DPP News Agency

DPP News Agency News and Updates
(1)

31/08/2025

Mwini wake wa Mtandire -mtsiriza constituency

mawa tilowele ku Lakeshore
31/08/2025

mawa tilowele ku Lakeshore

31/08/2025



Apolisi ku Machinga amanga a Mustafa Pongolani omwe akuimira chipani cha UTM ngati phungu kudera la kummawa kwa boma la Machinga powaganizira kuti adavulaza munthu komanso kuyambitsa chisokonezo.

Mneneri wa polisi mchigawo cha ku mmawa a Patrick Musa atsimikiza za nkhaniyi ndipo ati a Pongolani adamangidwa dzulo loweruka ndipo pano aturutsidwa pa belo.

A Musa ati omangidwawa akuwaganizira kuti adachitira za mtopola komanso kuvulaza mmodzi mwa otsatira chipani cha UDF omwe amkachoka ku msonkhano wa ndale pamodzi ndi yemwe akupikisana nawo pa mpando waphungu kuderali a Esther Jolobala usiku wa lachinayi.

Malinga ndi malipoti, a Pongolani pamodzi ndigulu lina la anthu adatchingira a Jolobala ndi gulu lawo ndikumawajambula kanema komanso kuwakuwiza kuti amachita zizimba zamatsenga.

Wolemba Blessings Tambala

pokayenela kuchonga
31/08/2025

pokayenela kuchonga

Malawi Elections Updates   newsHigh court ya Malawi yalamula Bungwe lothana ndizi phupu la ACB kuti lisiye kumuuopyeza V...
31/08/2025

Malawi Elections Updates
news

High court ya Malawi yalamula Bungwe lothana ndizi phupu la ACB kuti lisiye kumuuopyeza Vice President Dr Michael Usi ndipo a Vice President asapiteko Ku ACB

Bungweli linalamula A vice President kuti within 24 hours apezeke Ku ma office ao komanso atuluse ma Pepala onse amene Alinao oonesa akuba apo ai amangidwa .

High court yanena kuti kumeneko ndikumupasa mantha munthu cholinga asamayankhule mwa ufulu kotero
Muzapange zimenezo Zisankho zikadusa

Palibe amene angafikenso apa pa 52K viewers, this was on Times only, nde kunalinso ma page ena ambiri mbiri
31/08/2025

Palibe amene angafikenso apa pa 52K viewers, this was on Times only, nde kunalinso ma page ena ambiri mbiri

31/08/2025
31/08/2025

Wina ku statehouse wagula ndege ili ku China, akutelotu Onjezani Kenani. MCP ikupakulatu

31/08/2025

Mtandire -mtsiriza constituency mega rally

31/08/2025

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DPP News Agency posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share