Manzy Alfred

Manzy Alfred producer and artist
Soon we are going to open ....
Next level exclusive
WHY BE STAR Records

03/10/2025

Music ndichithu chokoma kwambiri kuyambila kwa artist ndikwaomvela

01/10/2025

anyday tipange zolowa live on this page ndikufotokozeleni zomwe zikundikanikisa kutsegula ku SA kuno sizofuna zanga koma kamba kazovuta zina koma kumbali yanga ndimayetsesa

26/09/2025

Chikondi chomwe mumandionetsela ma follows anga kwaine ndichokwanila ngati ndingopanga day yozagawa ya

25/09/2025

tayamba kale kunyezimila muulamulilo wa Arthur Peter Mutharika

24/09/2025

Kodi mukundimva ku mtengo uko?!! Eya, ndamumva wina akuti koma pammepo, koma pammepo, watii 🤣🤣🤣

24/09/2025

I got this 🤣🤣🤣

22/09/2025

Hello my beautiful people

09/09/2025

Akungi adya bwino sakumveka mawu. Akulingalira zoti mwina yonse angoisitika kapena agule tchipisi. 😅

Azerbaijan 1-1 Ukraine
France 2-1 Iceland
Armenia 2-1 Ireland
Hungary 2-3 Portugal
Bosnia 1-2 Austria
Cyprus 2-2 Romania
Norway 11-1 Moldova
Albania 1-0 Latvia
Serbia 0-5 England

09/09/2025

kZa Betway Mudya?
HT:
DR Congo 2-1 Senegal
South Africa 1-1 Nigeria
Burkina Faso 0-0 Egypt
Cape Verde 0-0 Cameroon
Togo 1-0
level Exclusive

16/08/2025

Tisangone tachivungeni chipemphero kumeneko ku

16/08/2025

Ngati mwadzuka bwino nenani zikoma kuli kumuthokoza Mulungu ena adzukila kuwawa mutu ena mimba zambiri zimatha kuchitika

Address

King William's Town

Telephone

+265980918133

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Manzy Alfred posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category