Nyasa Buzz

Nyasa Buzz Trending News and Entertainment

Ngati zaboza kuti uku ndi ku 25 ku Lilongwe
09/09/2026

Ngati zaboza kuti uku ndi ku 25 ku Lilongwe

Kodi ambiri akuti bwanji za Ekhaya Fc kumeneko
08/09/2026

Kodi ambiri akuti bwanji za Ekhaya Fc kumeneko

TIYENI TIYENI TIKAWODEMpaka K70,000ulendo wa ku tunduma watheka.
08/09/2026

TIYENI TIYENI TIKAWODE

Mpaka K70,000

ulendo wa ku tunduma watheka.

23/08/2026

KOMATU MWANAYU LUSO NDENDENDE CHAWINGA SISTERS.

Koma zinthu izizi ndizosangalatsa kwambili..Timasangalala chonchi tikamaonela ma team akunja but now we are celebrating ...
09/08/2026

Koma zinthu izizi ndizosangalatsa kwambili..
Timasangalala chonchi tikamaonela ma team akunja but now we are celebrating our own, this is beautiful
This is good news for Malawi.

If Algeria is not busy we can play tomorrow we are in a hurry we don't want to waste time Malawi the warm heart of Afric...
09/08/2026

If Algeria is not busy we can play tomorrow we are in a hurry we don't want to waste time Malawi the warm heart of Africa.

Go Malawi!!!
09/08/2026

Go Malawi!!!

Mkulu wa bungwe lowulutsa mau la Malawi Broadcasting Corporation (MBC), a Brian Banda wamwalira.Wofalitsa nkhani ku bung...
08/08/2026

Mkulu wa bungwe lowulutsa mau la Malawi Broadcasting Corporation (MBC), a Brian Banda wamwalira.
Wofalitsa nkhani ku bungwe la MBC a Chisomo Mwamadi watsimikizira tsamba la MBC Digital za imfayi.
A Mwamadi ati a Banda amwalira ku chipatala cha Mwayiwathu atadwala kwa nthawi yochepa.

01/08/2026

Malawi 1:0 Egypt

TEMWA UJATU NDAMENEYU, NDE MUZITI CHANINO???
28/07/2026

TEMWA UJATU NDAMENEYU, NDE MUZITI CHANINO???

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nyasa Buzz posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share