Aubrey Chilota

Aubrey Chilota John 15:3
[3] Now ye are clean through the word which I have spoken unto you.

31/07/2026
31/07/2026

Amene mukufunafuna uthenga oti mulemera nyengo zanu zisintha kenaka muziti Amen.
kazifunafunani koma mukhumudwa
chisawutso chitayambika inu osadyerera mkomwe komaso osalandira mkomwe
TIYENI tisamale

Shalom

31/07/2026

Uthenga wakulapa
1. mukulota mukugonana ndi anthu
2. mukuthamangitsidwa
3. MUKUDYA
4. MUKUMWA
5. muli kumadzi mukusambira
6. muli Kuma party
7. mukumenyana NDEWU
8. mukukwatira
9. mukufusira mkazi mpaka kulola
10. mukufusiridwa mpaka kulola

dziwani mukufunika kupemphereredwa ngati simutulakoma ndikuzafa muli mu izi inuyo wakugahena. kapena Yesu akamabwera inuyo mudzatsala ndithu.
funani funani mamasulidwe lero nthawi yatha.
shalom

30/07/2026

tokha sitingayende opanda Yesu
nkhondo sitingapambane

29/07/2026

1 Atesalonika 5: 17
pempherani kosalekeza

28/07/2026

usatope Pempherabe mpaka amve kulira kwako
Ambuye ndiwabwino akuyankhani

28/07/2026

kugona ndichizolowezi koma kudzuka ndizisomo Cha Mulungu

Address

Aquamuziq@gmail. Com
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Aubrey Chilota posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share