Mojar tech Kaweche

Mojar tech Kaweche Technology Settings Teacher
Content Creator

12/03/2025

Kodi Mukudziwa kuti m***a kumagwiritsa ntchito nambala ya dziko linalilironse lomwe mungafune pa Whatsapp!?

15/01/2025

Ngati Facebook account yanu mukudalira Password yokha dziwani kuti siyotetezeka ,ndipo akamberembere atha kukupangani chipongwe nthawi ina iliyonse .

Peweni kumapanga Click link iliyonse yomwe yabwera ku ma notification yanu.

Musapere ma details a Facebook yanu ngakhale atati amakudziwani

Tetezani Account yanu

30/12/2024

๐—ž๐˜‚๐˜๐—ถ ๐—ช๐—ต๐—ฎ๐˜๐˜€๐—ฎ๐—ฝ๐—ฝ ๐˜„๐—ฎ๐—ป๐˜‚ ๐—ฎ๐˜€๐—ฎ๐—บ๐—ฎ๐—ฝ๐—ฎ๐—ป๐—ด๐—ฒ ๐—ฑ๐—ผ๐˜„๐—ป๐—น๐—ผ๐—ฎ๐—ฑ ๐˜‡๐—ถ๐—ป๐˜๐—ต๐˜‚ ๐˜†๐—ฒ๐—ธ๐—ต๐—ฎ

18/12/2024

๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚Macheza abwanji awa

18/12/2024

MENE MUNGABISIRE CHART KU WHATSAPP

12/12/2024

Mene mungasungire zinthu zanu ku Google Drive

08/12/2024

Tetezani Account yanu ya Facebook


03/12/2024

Remove any Object from your picture

28/11/2024

GOOD MORNING LADIES AND GENTLEMAN

21/11/2024

How to upgrade 3 G Network to 4G Network

12/11/2024

Zina mwa zifukwa zomwe zimapangitsa phone yanu kumapanga zobalalika

Address

M1
Lilongwe Area 18

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mojar tech Kaweche posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share