MWHYPE

MWHYPE Artist
(8)

11/10/2025

🤣🤣🤣🤣🤣

Ak*t ndi nice tune 🔥🔥
11/10/2025

Ak*t ndi nice tune 🔥🔥

Mulungu awone kuyesesa kwanu ndipo adalise kulimbika kwanu amene🙏🙏🙏 coming soon 🙏🙏🙏prod. By Wilson Macia Ngwira and wathu

Awa inu
15/09/2025

Awa inu

22/08/2025

Komatu pitalayu boma ndilakedi🔥🔥🔥🔥🔥

13/08/2025

Tawafuseni abale 🤣🙌

Dr Michael usi   kuyankhulapo pakulandinda galimoto🤭🤭🤭🤣🤣🤣🔥🔥🔥🔥
13/08/2025

Dr Michael usi kuyankhulapo pakulandinda galimoto🤭🤭🤭🤣🤣🤣🔥🔥🔥🔥

Kwaolatu ayamba kuululana🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
12/08/2025

Kwaolatu ayamba kuululana🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

Kondwani kachamba writes:Zinazi put politics aside and chose to be a Malawian .Mzikhala anthu a Chilungamo.Is this a lie...
11/08/2025

Kondwani kachamba writes:

Zinazi put politics aside and chose to be a Malawian .

Mzikhala anthu a Chilungamo.

Is this a lie👇? Alipo wa MCP angakane mitengoi ?

Ngati mitengoyo ndi chilungamo then ndiwe munthu otani kumafunabe k*ti Amalawi next 5 years avutikebe? Are you normal ?

1. Cement 40 thousand koma akukwerabe

2. Feteleza 160 thousand akukwerabe
3. Chimanga 120 thousand mu January Pano 75 thousand
4. Nyama 1 Kg 15 thousand
5. Mafuta Ophikila 20 litres 130 thousand

Ndiye 5 years more k*ti zifike k*ti?

Guys mphamvu zosapota MCP zikuchoka k*ti anzathu with all these ? Honestly let's be real?

Ndiye k*ti Dziko lathu tikulifunila zabwino like for real?

Please be Patriotic for once and chose the truth .

Our Economy has been completely abused and destroyed and to make it worse there is no solution. They don't even know where to start from to fix our economy.

Am sorry I can't support izizi.

Mukanasamala anthuwa bwenzi tikuchemelera kwambiri k*ti Boma ndi lomweli! Koma izizi izi ai aaaaaa. Am sorry.

I love Malawi .

Beans tamazi samalani azimayi Zimaleveni zabwino koma kumango ziyalusa eeeish 🙌🙌🙌🙌🙌
10/08/2025

Beans tamazi samalani azimayi
Zimaleveni zabwino koma kumango ziyalusa eeeish 🙌🙌🙌🙌🙌

Kell Kay and Yo Maps Yo akukaithila 🔥🔥🔥🔥 ku motel galaden let's go guys
08/08/2025

Kell Kay and Yo Maps Yo akukaithila 🔥🔥🔥🔥 ku motel galaden let's go guys

08/08/2025

Awatu nyimbo amenya Jose J1 ft Moses makawa lin in comment

MCP yagulaa salu ndalama zambili mbili pamene solution yamafuta ikumavutabe koma kumwesa anthu maheu pa nsonkhano uyu at...
05/08/2025

MCP yagulaa salu ndalama zambili mbili pamene solution yamafuta ikumavutabe koma kumwesa anthu maheu pa nsonkhano uyu ati tukwanisa 😠😠😠😠😠

Address

Lilongwe

Telephone

+265883835651

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MWHYPE posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share