Roy View

Roy View Servant of GOD! MASO Awards Fashion Designer of the Year 2022
UMP Fashion Designer of the year 2018.
(1)

American Embassy African Day Best Outfit 2016
Reggae Dancehall Artist
Football Jerseys Designer
Sports Writer
Brand Promoter

Miyendo ya mpira sisowa....Ma team ambiri amandifuna vuto ndi signing on fee....sangakwanitse.
25/09/2026

Miyendo ya mpira sisowa....

Ma team ambiri amandifuna vuto ndi signing on fee....sangakwanitse.

Christopher Jacamah Kumwembe has confirmed that ......Eeish tidikire kaye ayambe kumenya game uyuyu mngosapanganika...Si...
25/09/2026

Christopher Jacamah Kumwembe has confirmed that ......

Eeish tidikire kaye ayambe kumenya game uyuyu mngosapanganika...

Sitipanganso confirm 😆

Flames ndiyathu....sitingaisiye. mzovuta kuisiya.Malawi Vs South Sudan (6pm)Koma anyamata a Sudan ndi atali atali chonde...
25/09/2026

Flames ndiyathu....sitingaisiye. mzovuta kuisiya.

Malawi Vs South Sudan (6pm)

Koma anyamata a Sudan ndi atali atali chonde ma player a Flames ikani mpira pansi lero komanso muzipanga njomba kwambiri and use short passes.

Ndanena ine coach wanu wa pa FB 😆

Readily available in the UK and in MalawiContact: +447466 438472 (Amos Phiri)
24/09/2026

Readily available in the UK and in Malawi

Contact: +447466 438472 (Amos Phiri)

Tachioneni 🤣Welcome back mphwanga!!!
24/09/2026

Tachioneni 🤣

Welcome back mphwanga!!!

Flames siopa height ....tithana nawo!
24/09/2026

Flames siopa height ....tithana nawo!

24/09/2026

🟢🟠 WELCOME, HASSAN! 🟢🟠

A new chapter begins. Welcome to Masters FC, Hassan!

24/09/2026

Mipikisano yambiri yomwe Malawi imapanga participate imapwetekeka ndi ma team awa:

1. Zambia (Football)
2. South Africa (Netball and Football)
3. Uganda (Netball and Football)

Timayenera kuwaika maiko amenewa ngati benchmark yathu ya success.

Study momwe amapangira develop mpira wawo and when we start beating them comfortably then tikhoza kumanena kuti masewera anthu ampira akuyenda.

Sikulakwa kuika beating these teams as our primary target in developing our football.

Poyamba Zambia football imapanga develop bwino chifukwa cha youth development yawo koma pano akutsika chifukwa cha age cheating.....

Of course South Africa is becasue of money....

But we can do something.

23/09/2026

That's why azibambo sitikhalitsa 😂

23/09/2026

Malawi 1-1 Comoros

90+ rescue

Address

Box 94
Lilongwe
0000

Telephone

+265999685678

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Roy View posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Roy View:

Shortcuts

Share