Malawi Infotainment Site

Malawi Infotainment Site Promote | Upload Music | Entertainment Website
For Advertise & Promo 0887777722
(1)

Anthu akungokamba  ya Leah Malekano🙌 ichiso muli kulimba mtima ndi mzeru
20/09/2025

Anthu akungokamba ya Leah Malekano🙌 ichiso muli kulimba mtima ndi mzeru

20/09/2025

Zotsatila zachisankho zobvomelezeka
ku
Lutchenza Manicipaliry
Dr Chakwera 336
Prof Mutharika 7547

Kasungu Manicipality
Prof Mutharika 8818
Dr Chakwera 7831

Mwanza
Dr Chakwera 2228
Prof Mutharika 30,576

Likoma
Prof Mutharika 4177
Dr Chakwera 1817


20/09/2025



ADAD AKUTSOGOLA

Malingana ndi zotsatira zotsimikizika ndi bungwe la MEC, zotsatira kuchokera ku Makhonsolo a Likoma, Kasungu Municipality, Luchenza ndi Mwanza, mtsogoleri wachipani cha Democratic Progressive (DPP), Professor Arthur Peter Mutharika ndi amene akutsogola ndi mavoti 50,131, Dr Lazarus Chakwera achipani cha Malawi Congress (MCP) ali ndi mavoti 13,199 ndipo a Dalitso Kabambe achipani cha UTM pano ali ndi mavoti 3,939.

Izi ndi malingana ndi Wapampando wa bungwe la MEC, Justice Annabel Mtalimanja yemwe wangomaliza kumene kupangitsa msonkhano wa atolankhani.

Kaya Wafufutilanji post iyi Kondwani
19/09/2025

Kaya Wafufutilanji post iyi Kondwani

19/09/2025

Dr Hastings Kamuzu Banda chaka cha 1994 anabvomeleza kuti aluza ma vote asanathe kuwelengetsa

Dashboard nde ambili ayiwona kale
19/09/2025

Dashboard nde ambili ayiwona kale

All is set for the press briefing at MCP HeadquartersAkuti Aberedwa 🙌
19/09/2025

All is set for the press briefing at MCP Headquarters

Akuti Aberedwa 🙌

MACRA yachosa Website ya Luntha TV yomwe anapanga upload Dashboard ya Presidential Election results
19/09/2025

MACRA yachosa Website ya Luntha TV yomwe anapanga upload Dashboard ya Presidential Election results

 Kuli chitetezo chokhwima pomwe asilikali ankhondo ayamba kuchuluka ku BICC  komwe ntchito yowunikira zikalata zachisank...
19/09/2025



Kuli chitetezo chokhwima pomwe asilikali ankhondo ayamba kuchuluka ku BICC komwe ntchito yowunikira zikalata zachisankho ikuchitika.

Chiwerengero cha asilikalichi chikuchuluka pomwe zotsatira za maboma ndi madera osiyanasiyana zikupitilira kufika mchipinda momwe zikuwunikidwa.

19/09/2025




NTCHEU PRESIDENTIAL AND PARLIAMENTARY SUMMARY

1. Peter Mutharika (DPP): 106917
2. Dalitso Kabambe (UTM): 14270
3. Lazarus Chakwera (MCP): 9063

District Total valid votes: 136888
District Total void: 3695
District Total votes: 140584
District
Total Registered: 172874

PARLIAMENTARY (Presumed Winners)

1. *Ntcheu Central Central East Constituency* - Norman Chisale (DPP) 10654 votes
Total Registred: 18332
Total voted: 15663
Total valid:15281
Told void: 382

2. *Ntcheu North West Constituency*- Joseph Malinga moyo (Independent) 5819
Total Registred: 19279
Total voted: 15691
Total valid:15271
Told void: 420

3. *Ntcheu Central*- Paul Wongani Ng'oma (Independent) 7208

Total Registred: 24088
Total voted: 19179
Total valid:18769
Told void: 428

4. *Ntcheu Bwanje Constituency* - Thom Chigona (DPP) 4851

Total Registred: 27376
Total voted: 22140
Total valid:21627
Told void: 513

5. *Ntcheu South Constituency* - Edgar Wisdom Kapalamula (Independent) 11828

Total Registred: 22115
Total voted: 18028
Total valid:17563
Told void: 465

6. *Ntcheu North Constituency* - Mandela Gomez (DPP) 8379

Total Registred: 21313
Total voted: 17148
Total valid:16721
Told void: 427

7. *Ntcheu North West* -Joseph Malingamoyo (Independent) 5819

Total Registred: 19279
Total voted: 15691
Total valid:15271
Told void: 420

8. *Dzonzi Mvai Constituency* - Dyles Moses Mbengo (Independent) 4579

Total Registred: 17663
Total voted: 14547
Total valid:14111
Told void: 436

19/09/2025

Summary of Salima Parliamentary Results

Unofficial Results

Salima Central Constituency
Gerald Kapisen Phiri (MCP) - 8, 374

Salima Central West Constituency
Enock Phale (Indipendent) - 13, 895

Salima South Linthipe Constituency
Joshua Maxwell Chizeze (Independent) - 5, 985

Salima North Constituency
Maxwell Edward Mnjemu (MCP) - 14, 285

Salima South Constituency
Madalitso Mazombwe (Independent) - 4, 698

Central East Constituency
Joel Chigona (DPP) - 4, 896

19/09/2025

SUMMARY OF THYOLO DISTRICT AND LUCHENZA MANICIPALITY CONSTITUENCIES PARLIAMENTARY UNOFFICIAL RESULTS.

1. LUCHENZA MANICIPALITY CONSTITUENCY
Chimwemwe Chipungu (DPP) 2,572

2. THYOLO GOLIATI CONSTITUENCY
Moreen Namwali (DPP) 17,316

3. THYOLO CENTRAL CONSTITUENCY
Ben PHIRI (DPP) 26,788

4. THYOLO MASAMBANJATI CONSTITUENCY
Flavia Custom (DPP) 5,861

5. THYOLO MIKOLONGWE CONSTITUENCY
Timothy Sukali (DPP) 9,959

6. THYOLO KHONJENI- MANGUNDA CONSTITUENCY
Hastings Kajomba (Independent )19,941

7. THOLO THAVA CONSTITUENCY
Mary Thom Navitcha (DPP) 32,005

8. THYOLO THEKERANI CONSTITUENCY
Mavuto Sandram Scott (DPP) 9,543

9. THYOLO BVUMBWE -MASENJERE CONSTITUENCY
Charles Mchacha (DPP) 11,872

Promoting Malawian Movies & Arts

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Infotainment Site posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Malawi Infotainment Site:

Share