06/08/2026
nthawi zonse pamene tikukhala tidzikhalaso ndi chikondi pozindikila kuti anayamba kutichitila chikondi ndi mulungu, Pali anthu wena pakati pathu azathu akalakwitsa timayankhula modutsa mulingo, sitisamala za azathu poganiza ngati zathu zose zili bwino ,Koma sitizindikila kuti palibe amene zake zili 100% tonse tili ndizofoka zimene zikufunika mulungu kuti adzitikhululukila kufikila kubwela kwa ambuye ,onani verse lli👇
Luka 8 verse7 aphuzitsi amalamulo ndi afalisi anabweletsa mkaz amene anagwidwa akuchita chigololo. lwo anamuyimililitsa patsogolo pa wanthu 4 ndipo anati kwa yesu," aphuzitsi , mkazi uyu tinamugwila akuchita chigololo.4 mmalamulo amose anatilamulila kuti akazi otele tiwagende miyala. tsonopano lnu mukutipo kuti chani?
pamene lwo anapitilila kumufusa, lye anawelamuka ndipo amawuza kuti , ngati wina wayinu alipo opanda tchimo ,ayambe lye kumugenda miyala mkaziyu,"lye anawelamaso pasi ndikulemba padothi, 8 lwo atamva lzi anayamba kuchoka mmodzi mmpdzi
mateyo 7 verse 1 musamaweluze wena ,kuti nanuso mungadzaweluzidwe.2 pakuti momwemo lnu muweluzila wena ,lnuso mudzaweluzidwa chimodzimodzi
tawonani amene anabweletsa mkazi wachigololowo pamene yesu adawawuza kuti ngati alipo mmodzi wayinu amene alibe tchimo lye ayambe kumugenda miyala mkazi yu, koma atamva lzi anayamba kuchoka okha chifukwa chani anayamba kuchoka chifukwa zinalipo zina zimene zimawoneka ngati zing,Ono zing,Ono koma zimakhalabe kuti ndi tchimo pamaso pa mulungu, choncho pamene tawona kuti wina wake walakwila kaya dziko kaya lnuyo tiyeni tisamale kalankhulidwe kathu ndikachitidwe kathu pozindikila kuti nafe tili nazo zofoka zimene kumaso kumaso kwa dziko lapasi ndizosawonekela koma pamaso pa mulungu ndizowoneka, palibe salakwitsa choncho chikondi patsogolo ambuye akutsogoleleni muzonse muzonse