MLIMI FELIE

MLIMI FELIE Young Agriculturalist, Hustler in Agriculture, Agriculture service provider

GOD IS GREAT Happy plus ➕ONE 🎂🎂to meMLIMI FELIE 🌱 thanks mom n dad ❤️thanks Bwana Miyuzi for the gift of birthday artwor...
12/07/2026

GOD IS GREAT Happy plus ➕ONE 🎂🎂to me
MLIMI FELIE 🌱
thanks mom n dad ❤️
thanks Bwana Miyuzi for the gift of birthday artwork, mwandilemekeza broo God bless, real recognize real 👑

Onion Nursery
09/07/2026

Onion Nursery

ATATE FARMS will help you. Yambanipo
09/07/2026

ATATE FARMS will help you. Yambanipo

Zomayiphonya
09/07/2026

Zomayiphonya

Clean Money Dirty hands AGRICULTURE ASEH eeeeti bwaaZIMANGOFUNIKA kuyamba
08/07/2026

Clean Money Dirty hands
AGRICULTURE ASEH
eeeeti bwaa
ZIMANGOFUNIKA kuyamba

Kunja kukangocha umangoziwilatu kuti kwachela pakalapakala😃...Paja ndimagwilatu ntchito zingapo ndekha🙈Yau CEO 👨‍💼Market...
30/06/2026

Kunja kukangocha umangoziwilatu kuti kwachela pakalapakala😃...

Paja ndimagwilatu ntchito zingapo ndekha🙈

Yau CEO 👨‍💼
Marketer
Farm Manager
Electrician 👨‍🔧
Carpenter 👷‍♂️🪚

Apa ndimagwila ngati Mnyamata wa a electrician 😂😂😂🙌

Good morning 🙂

Pena kumasewerako ndi ziweto osangoti maturity nthawi zonse😅 boiz kuionetsa
30/06/2026

Pena kumasewerako ndi ziweto osangoti maturity nthawi zonse😅
boiz kuionetsa

M'limi Felie tiyambe chonchi till we make it
30/06/2026

M'limi Felie tiyambe chonchi till we make it

Anthu akuionetsa zimangofunika kuyamba
30/06/2026

Anthu akuionetsa zimangofunika kuyamba

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MLIMI FELIE posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share