Chinsapo Entertainment & Promotion Hub

Website

Chinsapo Entertainment & Promotion Hub Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Chinsapo Entertainment & Promotion Hub, Digital creator, Lilongwe.

๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผCHINSAPO ENTERTAINMENT & PROMOTION HUB Kodi
๐ŸŽค Ndiwe artist?
๐Ÿ›๏ธ Uli ndi business?
๐ŸŽง DJ, MC kapena dancer?
๐ŸŒŸ Uli ndi talent?
๐Ÿ’ฏ Bwera pa CHINSAPO ENTERTAINMENT & PROMOTION HUB โค๏ธ๐Ÿ˜๏ธ
Tikukupatsani FREE PROMOTION ndi support ya kwathukuno ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ

Chinsapo Entertainment & Promotion Hub@topfansAnthu okwiya apha ndi kuwotcha bambo wina yemwe sakudziwika pakadali pano ...
30/09/2026

Chinsapo Entertainment & Promotion Hub@topfans

Anthu okwiya apha ndi kuwotcha bambo wina yemwe sakudziwika pakadali pano pomuganizira kuti anaba ng'ombe mmudzi wa Kamsonga m'dera la mfumu yayikulu Malenga m'boma la Ntchisi.

Yemwe watitsina khutu za nkhaniyi, wati usiku wapitawu, woganizilidwayu ndi anzake ena omwe athawa pakadali pano, anapita mmudziwo pa galimoto la Honda Freed (NN10384) ndi kuba ng'ombe 13 ndipo 6 anazipha kale pomwe 7 zikadali za moyo.

Anthu ena omwe anaona anthuwa akukusa ng'ombezi mu msewu wa Mbuyedziko-Gwangwa, anadziwitsa anthu mmidzi yozungulira omwe anayamba kuthamangitsa mbavazo ndikugwira dalayivala wa galimotoli yemwe ananumenya ndi kumuwotcha limodzi ndi galimotolo.

Pakadali pano, wofalitsa nkhani za apolisi m'bomali a Salomy Zgambo, ati tiwapatse nthawi kuti afufuze kaye za nkhaniyi.

Nkhani Yomvetsa Chisoni๐Ÿ’”__ Carver Bhima,yemwe anali Founder komanso Mwini wa License ya Miss Malawi kwa zaka zambiri, wa...
29/09/2026

Nkhani Yomvetsa Chisoni๐Ÿ’”
__ Carver Bhima,yemwe anali Founder komanso Mwini wa License ya Miss Malawi kwa zaka zambiri, wamwalira atadwala matenda a impso (kidney).

Bhima anali wodziwika kwambiri pa ntchito yokonza ndi kuyendetsa mpikisano wa Miss Malawi,ndipo kwa zaka zambiri anathandiza kulimbikitsa za kukongola ndi luso la atsikana mโ€™dziko muno.

Mzimu wake uwuse mumtendere๐Ÿ•Š๏ธ

Bambo Wiz Chimodzi, aku Mzimba, azipha pomwa chiphe (poison) kutsatira kuthetsa chibwenzi komwe anapanga girlfriend wake...
28/09/2026

Bambo Wiz Chimodzi, aku Mzimba, azipha pomwa chiphe (poison) kutsatira kuthetsa chibwenzi komwe anapanga girlfriend wake yemwe dzina lake ndi Sithembire.

Asanamwe mankhwala wo, Wiz anayimba kaye nyimbo yoti uzandisowa, kenaka kupanga post mkazi yo pa Facebook account yake, kenaka ndikumamwa poison.

Zikumveka kuti mkazi yo anapanga reconcile ndi ex boyfriend wake zimene zinapangitsa kuti Wiz asweke mtima

๐Ÿ“ข TIKUFUNA KUPANGA BUSINESS NDI INU!Kodi muli ndi katundu wa zakudya koma mukusowa msika wokhazikika woti mugulitsire? K...
28/09/2026

๐Ÿ“ข TIKUFUNA KUPANGA BUSINESS NDI INU!
Kodi muli ndi katundu wa zakudya koma mukusowa msika wokhazikika woti mugulitsire? Kapena mukufuna katundu wabwino komanso wodalirika woti tizigula nthawi zonse?
Tikufuna kugwirizana ndi anthu omwe ali ndi: Nkhobwe โ€ข Nandolo โ€ข Adyo โ€ข Bonya โ€ข Usipa โ€ข Ginger โ€ข Chidede โ€ข Mpunga โ€ข Onion
Sikuti tikufuna business ya tsiku limodzi ayi. Tikufuna mgwirizano wokhazikika komanso wodalirika, pomwe tidzagulirana katundu nthawi ndi nthawi, kutengera mtengo, kuchuluka komanso kupezeka kwa katundu.
Ngati muli supplier kapena muli ndi katundu wochuluka ndipo mukufuna msika, tilumikizane.
๐Ÿ“ Lilongwe, Chinsapo โ€” Near UNICEF Ground
๐Ÿ“ž 0997 043 383
Tiyeni tigwirizane, tigulitsane komanso tipindule tonse.

We can confirm now Hiphop Star, Fredokiss confirms he will release โ€˜Ghetto Angelโ€™ music video ft GD & WG on Monday ๐ŸŽ™๏ธ
25/09/2026

We can confirm now Hiphop Star, Fredokiss confirms he will release โ€˜Ghetto Angelโ€™ music video ft GD & WG on Monday ๐ŸŽ™๏ธ

Uthenga wachisoni..kwa athu akwa Chinsapo lilongwe ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญKwa amene timamudziwa Emmanuel Mphonongo, mamuna wake wa Tsanzo N...
25/09/2026

Uthenga wachisoni..kwa athu akwa Chinsapo lilongwe ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

Kwa amene timamudziwa Emmanuel Mphonongo, mamuna wake wa Tsanzo Nyoni, watisiya pompano usiku omweuno. Emmanuel ndi mwana wa Mayi Mphonongo eni ake a Havanna Boutique pafupi ndi Tachira clinic.

Program sinadziwike chifukwa nanenso akundiuza chakumene....

Mzimu wa Emmanuel uwuse mu mtendere.... Pepani pepani..

Zomwe zikuchitika Ku Malawi ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ ndi Zomvesa chisoni kwambiri ๐Ÿ’” kuchotsa Moyo wa munthu nkumubela njinga nkuuzunzanso mtem...
25/09/2026

Zomwe zikuchitika Ku Malawi ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ ndi Zomvesa chisoni kwambiri ๐Ÿ’” kuchotsa Moyo wa munthu nkumubela njinga nkuuzunzanso mtembo wake kuuika mu plastic nkuulowesa mu baketi nkutaya pa ntchire anthu aziti ndi tomato ๐Ÿ˜ญ...osangoba njingayo bwanji chotengeranso Moyo ndi chani ๐Ÿคท?

Bambo Yamikani Hussein, azaka 29, omwe amapanga business ngati wakabaza WA njinga ya moto, apezeka ataphedwa ku Chigumula ku Blantyre, thupi lawo atalikulunga mu chi plastic ndikuwaponya pa tchire.

Zomvesa chisoni kwambiri akabanza akutha ๐Ÿ’”๐Ÿ˜ญ

๐Ÿ๐Ÿ”ฅ ELI NJUCHI โ€” โ€œGOATโ€ FT. KING PING ร— EL QUTRO ร— ACROAD TING ๐Ÿ”ฅ๐ŸKuchokera mu album yake yotchedwa MAGA ๐Ÿ’ฟ๐Ÿ”ฅAmasungila BOMB...
25/09/2026

๐Ÿ๐Ÿ”ฅ ELI NJUCHI โ€” โ€œGOATโ€ FT. KING PING ร— EL QUTRO ร— ACROAD TING ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ

Kuchokera mu album yake yotchedwa MAGA ๐Ÿ’ฟ๐Ÿ”ฅ

Amasungila BOMBA ili! ๐Ÿ’ฃ๐Ÿ˜ญ
Ine ndadziwa mochedwa kuti ma Slime anapha nyimbo iyi! ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

โ€œGOATโ€ si nyimbo chabe โ€” ndi presentation ya Hip-Hop legacy, yokhala ndi ma bars, energy komanso chemistry ya ma artist omwe akudziwa zomwe akuchita. ๐ŸŽค๐Ÿ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ

๐ŸŽง NOW AVAILABLE ON YOUTUBE ๐Ÿ”Š
๐Ÿ‘๐Ÿฝ Like โ€ข ๐Ÿ”” Subscribe โ€ข ๐Ÿ”„ Share

๐Ÿ‘‡๐Ÿฝ LISTEN HERE:
https://youtu.be/IGe1gCrQ2sY?si=vkTgrvCTnYfHYBUA

Support Malawi Hip-Hop ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ”ฅ
MAGA ๐Ÿ’ฟ | GOAT ๐Ÿ | HIP-HOP LEGACY ๐ŸŽค

Katundu takatenga yatsala ndi mitundu iyi tiyakhulen 0997043383 remember paja ikakhala business yakutali timatumiza koma...
25/09/2026

Katundu takatenga yatsala ndi mitundu iyi tiyakhulen 0997043383 remember paja ikakhala business yakutali timatumiza koma around lilongwe timapanga tokha deriver nsaluso zilipo tiyakhulen Chinsapo Entertainment

Address

Lilongwe
STUCCI

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chinsapo Entertainment & Promotion Hub posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share