NKhawa Njee’

NKhawa Njee’ Arts and Entertainment
(1)

18/09/2026

Apolice apha zika zakumalawi 4 populumutsa zika yaku Britain Imodzi, , 🥴🥴🥴🥴

Kulikonse Timatumiza😂🤣
18/09/2026

Kulikonse Timatumiza😂🤣

18/09/2026

Akuti Cyber 1 Ndidolo Opanga Hack Ma account Samalani ndi tima 2Pin kuma Account kwanuko Anali Msilikali kalero Asanayambe kuwabela anthu mma Bank mu Koma Tanvetsedwa Sabela ovutika ai amabelatu kuma Bank akamawelengela Ma Profit🤣😂

18/09/2026

The DC Bon Kalindo Once Said 👇🏾👇🏾

Akutitu wabwelera kuDen ngt anachitila Waku Crossloads uja nde Popeza waku Crossloads uja aPolice mpaka pano Akanafufuza...
17/09/2026

Akutitu wabwelera kuDen ngt anachitila Waku Crossloads uja nde Popeza waku Crossloads uja aPolice mpaka pano Akanafufuza ndekuti za Uyuyu tidikile 2028 Akufufuza Koma ife ZATINYANSA NDIPO NDIZOPUSA COZ 30 Million ija palibe walandila Sinanga wabwelera yekha Eeeeeh Anyamata mu Ndilande angogwilizana kt amugwire ndiiwowo 30 Mita isangopita Sizoona 🤣😂🤣😂🤣

Off the wall of Tamia Ja:Dear Dr Lazarus Chakwera, Mu nthawi yanu bwana magetsi samazima eeee pano sizilibwino. Komabe I...
17/09/2026

Off the wall of Tamia Ja:

Dear Dr Lazarus Chakwera,
Mu nthawi yanu bwana magetsi samazima eeee pano sizilibwino. Komabe I know kuti ndinayakhula zambiri chifukwa it’s a job kumalawi kuno kulibe ntchito olo ulimi akumapindula ndi athu ena omwe anathawa kulima .Komabe receive your flowers 💐munthu samayipa pa Zonse.

Komabe 2030 never again

Atangooneka ku Chikangawa pa 10 June 2024 anyamata aMCP awa Omwe amakhala Kwa Nsundwe Ndinangodziwilatu Anthu aja anagog...
17/09/2026

Atangooneka ku Chikangawa pa 10 June 2024 anyamata aMCP awa Omwe amakhala Kwa Nsundwe Ndinangodziwilatu Anthu aja anagogodeda awa ndianyamata amapha anzawo coz of Chipani Ainu wake amati NSUNDWE BARRACKS

16/09/2026

Umboni Wanjinso Mungafune after apapa MCP amwene tidzisemphana pa Ndale koma Zisamafike Pophana Eeeish😭😎💔

aMCP mmanama Mulungu Si Jemusi Lero Ntchito Yofufuza Yayamba LETS GIVE FLOWERS 💐 TO MAI MKANDAWIRE
16/09/2026

aMCP mmanama Mulungu Si Jemusi Lero Ntchito Yofufuza Yayamba LETS GIVE FLOWERS 💐 TO MAI MKANDAWIRE

Mmai yu akufotokoza bwinobwino akulakwitsa ndiofunsa mafunso Akufunsa Zopoila
16/09/2026

Mmai yu akufotokoza bwinobwino akulakwitsa ndiofunsa mafunso Akufunsa Zopoila

Address

Lilongwe
LCITY

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when NKhawa Njee’ posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share