Mugeta kingdom

Mugeta kingdom Artists
(3)

Akupepesa uku
27/08/2025

Akupepesa uku

πŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™Œ
27/08/2025

πŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™Œ

Khalizima ndi kineyo
31/07/2025

Khalizima ndi kineyo

Zomwe wayankhura Rema waswa mitima ya atsikana ambiriπŸ™ŒπŸ»Oimba wa ku Nigeria Rema wati iye zosaugwira mtima akaona skirt i...
28/07/2025

Zomwe wayankhura Rema waswa mitima ya atsikana ambiriπŸ™ŒπŸ»

Oimba wa ku Nigeria Rema wati iye zosaugwira mtima akaona skirt ikudutsa sakupanga nawo Ndipo iye akuti akadali wachinyamata ndipo safuna kutaya mphamvu zake pa atsikana

Malingana ndi Rema akuti padakalipano wakwanitsa kukhala Chaka chimodzi opanda kuchita zakusaweruzika ngakhale kiss or Hug amene Masiku ano akumamupewa iye wanenesa kuti focus yake ndiyongofuna kupanga ndalama basi

Road manager wake wasimikiza izi Ndipo wati nthawi iliyonse Rema akamaliza kuchita show, amangopita direct kunyumba kwake Sakhala ndi chidwi ndi ma after party kapena kusangalala ndi akazi ayi

Akakumana awa pamakhala pavuta πŸ™Œ
25/07/2025

Akakumana awa pamakhala pavuta πŸ™Œ

Kwachema πŸ˜‚
25/07/2025

Kwachema πŸ˜‚

Akamati Hitmaker:- Afana Ceez alandile ulemu ochuluka.Kukubwela chinatu oho
24/07/2025

Akamati Hitmaker:- Afana Ceez alandile ulemu ochuluka.
Kukubwela chinatu oho

πŸ˜‚
17/06/2025

πŸ˜‚

17/06/2025
Woman crush Wednesday
15/01/2025

Woman crush Wednesday

11/01/2025

Kodi mukuti zikukhala bwanji ?

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mugeta kingdom posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mugeta kingdom:

Share