10/06/2026
Nkhani yabwino kumangachi
BREAKING NEWS 📌
🚨💬Mtsikana yekhayo amene akulemba nawo mayeso a Standard 8 pasukulu ya Mangale Primary school ku Mangochi.
Akuti kuyambila 2017 mpaka 2025 pasukulupo palibe mwana wamkazi amene anafika Std 8 onse amasiila panjila chifukwa ena amakhala atenga mimba.