Mpesamalawi

Mpesamalawi The ministry supports Seventhday Adventist Music Ministries, financially and spiritually. We distribute and sale Adventist songs (videos and audios).

07/11/2025

mkati mwenimweni mwa tsiku lokozekela Sabbath amweneπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™Œ

πŸ₯³πŸ₯³πŸ₯³πŸŽ‰
mawa tikukapembedza kuti mwinatu mukumana ndi Mpesamalawi ohooπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Tikuterotu kuti Gululu walero anachitikila Ku salima  -day_Adventistkukukomatu km kutentha eessshiiii ...tikanya lunch t...
18/10/2025

Tikuterotu kuti Gululu walero anachitikila Ku salima
-day_Adventist

kukukomatu km kutentha eessshiiii ...tikanya lunch tingoseselekela m'Chigubimu bas kukasamba iyaaaπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ‘‹


Mpesamalawi

Dzuwa Liri kulowa//Mulungu atiputse//Ee Linda ndikupemphera//Mene nyali zili kuwala m,mwamba... πŸ™πŸ™ Mpesamalawi
17/10/2025

Dzuwa Liri kulowa//
Mulungu atiputse//
Ee Linda ndikupemphera//
Mene nyali zili kuwala m,mwamba...

πŸ™πŸ™
Mpesamalawi

11/10/2025

You fought the good fight πŸ˜­πŸ˜­πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”πŸ’”

😭😭

MUBAS Lecturer Dies After Long IllnessMalawi University of Business and Applied Sciences (MUBAS) community is saddened w...
11/10/2025

MUBAS Lecturer Dies After Long Illness

Malawi University of Business and Applied Sciences (MUBAS) community is saddened with the passing of Mr. Collins Namakhwa, a respected lecturer and researcher.

He passed away today after a long illness. Mr. Namakhwa was also an evangelist with the Seventh-day Adventist Church and was known for his dedication, warmth, and service both on and off campus.

Our thoughts and prayers are with his family during this difficult time. May his soul rest in peace.πŸ•ŠοΈπŸ•ŠοΈπŸ•ŠοΈπŸ•ŠοΈ

happy birthday to Eager Wellington Darlington Mponda πŸ“ΈπŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚ more years of serving LordMpesamalawi Wellington Darlington Mp...
10/10/2025

happy birthday to Eager Wellington Darlington Mponda πŸ“ΈπŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽ‚ more years of serving Lord

Mpesamalawi Wellington Darlington Mponda

Admin....ikufupan kuseliku πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Top fan olimba mtima amabwera poyela ndikusangalalira limoz ndi Mpesamalawi it's  's Birthday πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽˆ happy birthday πŸŽ‚ boss ...
05/10/2025

Top fan olimba mtima amabwera poyela ndikusangalalira limoz ndi Mpesamalawi it's 's Birthday πŸŽ‚πŸŽ‚πŸŽˆ

happy birthday πŸŽ‚ boss
Mpesamalawi

week yathai Mpesamalawi inali Ku Mwalawankhondo SDA Church lero yangoombokera tsidya la nsewu kufika pa Dauya SDA church...
04/10/2025

week yathai Mpesamalawi inali Ku Mwalawankhondo SDA Church lero yangoombokera tsidya la nsewu kufika pa Dauya SDA church Ku Dedza komweko .....takomedwako ndithobwa lakumeneko mbon ndi Orion Singers

happy Sabbath πŸ™

04/10/2025

afternoon kumeneko Sabbath ikuyenda bwa .....timvere iyiii nyimbo yabwino

Tsiku lokoma πŸ₯³πŸ₯³πŸ₯³πŸ₯³
27/09/2025

Tsiku lokoma πŸ₯³πŸ₯³πŸ₯³πŸ₯³

Mpesamalawi yakafika tsopano komwe Ku   komwe Glorious Hope Music Ministries ikutumikila ....  Lina Mpesamalawi izakupez...
13/09/2025

Mpesamalawi yakafika tsopano komwe Ku komwe Glorious Hope Music Ministries ikutumikila ....

Lina Mpesamalawi izakupezani kwanuko get ready πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Sabbath

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mpesamalawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mpesamalawi:

Share

Category