Jay Marz

Jay Marz Let's discuss daily life events ����

Palibe chinthu chowawa kwambir Ngati kuluza makolo 😭😭Ngati makolo Anu alimoyo tangonenani zikomo ambuye 🙏🙏🙏🙏 Follow Jay ...
07/05/2026

Palibe chinthu chowawa kwambir Ngati kuluza makolo 😭😭

Ngati makolo Anu alimoyo tangonenani zikomo ambuye 🙏🙏🙏🙏

Follow Jay Marz

Tikakwera magimoto pa maulendo osiyasiyana nkusikamo wamoyo Tizingoti zikomo ambuye 🙏🙏🙏🙏🙏Anthu akumwalira tsiku ndi tsik...
02/05/2026

Tikakwera magimoto pa maulendo osiyasiyana nkusikamo wamoyo
Tizingoti zikomo ambuye 🙏🙏🙏🙏🙏
Anthu akumwalira tsiku ndi tsiku ndi Ngozi zapansewu 😭😭😭😭😭


Follow Jay Marz

Zinthu Zooneka Ngati Chikondi...✍🏽• Kugonana• Kuyimbirana foni nthawi zonse• Kudalirana/kusamaliridwa• Kutuluka limodzi ...
30/04/2026

Zinthu Zooneka Ngati Chikondi...✍🏽
• Kugonana
• Kuyimbirana foni nthawi zonse
• Kudalirana/kusamaliridwa
• Kutuluka limodzi nthawi zonse
• Zithunzi pa malo ochezera a pa Intaneti
• Mphatso ndi ndalama

Chimene Chikondi Chilidi...✍🏽
• Ulemu
• Kukhululuka
• Kudalirana
• Kudzipereka
• Kuthandizana
• Zolinga zofanana
• Kukula limodzi
• Kukambirana mochokera pansi pa mtima
• Kukondana m'maganizo komanso mwakuthupi

Ngati muyenera kupitiriza kuuza mnzanu zomwezo za momwe mukumvera mobwerezabwereza, ndipo palibe chomwe chimasintha, dziwani kuti sakulemekezani. Sikuti chifukwa sakukumvani—ndi chifukwa sakufuna kukumvani.
Tikunvana kumbuyoko🤔🤔🤔🤸🤸🤸🤔🤔🤔🤔
Follow Jay Marz

Aliyense mmoyo Uno amakhala ndi chokhumba 🤔🤔🤔 Kumbukilani kumapempherera chokhumba chanu tsiku ndi tsiku Kuti mulungu ak...
28/04/2026

Aliyense mmoyo Uno amakhala ndi chokhumba 🤔🤔🤔
Kumbukilani kumapempherera chokhumba chanu tsiku ndi tsiku Kuti mulungu akwanilitse
🙏🙏🙏🙏🙏
Follow Jay Marz

So sad 😭😭😭😭 Walimbana nako kulimbana kwabwino 😭😭😭
27/04/2026

So sad 😭😭😭😭
Walimbana nako kulimbana kwabwino 😭😭😭

RIP  mzimu wako uuse muntendere 😭😭😭😭😭Davie wamwalira anavutika ndi cancer Ambuye atonthoze akubanja kwawo
27/04/2026

RIP mzimu wako uuse muntendere 😭😭😭😭😭
Davie wamwalira anavutika ndi cancer
Ambuye atonthoze akubanja kwawo

Utsiku kunali nkhondo zambiri Koma watizusabe ndi Moyo 😀😀😀🤥🤩🤩🤩🤗🤗🙏🙏🙏🙏Follow Jay Marz
26/04/2026

Utsiku kunali nkhondo zambiri Koma watizusabe ndi Moyo 😀😀😀🤥🤩🤩🤩🤗🤗🙏🙏🙏🙏
Follow Jay Marz

ZAKA CHIKWI- KUONONGEDWA KWA DZIKO LAPANSI Nthawi yobwera Khristu, akufa olungama adzauka, pamodzi ndi olungama amoyo ad...
25/04/2026

ZAKA CHIKWI- KUONONGEDWA KWA DZIKO LAPANSI

Nthawi yobwera Khristu, akufa olungama adzauka, pamodzi ndi olungama amoyo adzakwatulidwa kukakumana naye mu mlengalenga. Pamenepo oyipa adzafa poona ulemelero wake (1 Atesalonika 4:16,17; 2 Atesalonika 2:8).
Kwa zaka chikwi dziko lapansi lidzakhala bwinja (Yeremiya 4:23-26)

Satana adzayendayenda pa dziko lowonongeka, kulingalira za zotsatira za kupanduka kwake. Adzavutika atalandidwa mphamvu ndipo sipadzapezeka oti amunyenge (Chivumbulutso 20: 1-3)
Mu zaka chikwi'zi, olungama adzalamulira ndi Khristu kumwamba ndikuchita ntchito yakuweruza. Adzaweruza oyipa ndi angelo akugwa, kuyerekeza zochita zawo ndi lamulo la Mulungu ndi kutsimikizira chilango choyenera pa mlandu uliwonse. ( Chivumbulutso 20:4; 1 Akorinto 6:3)

Kumapeto kwa zaka chikwi, mzinda Woyerawo udzatsika kuchokera kumwamba (Chivumbulutso 21:2), anthu oyipa adzaukitsidwa mu mdzukiro wachiwiri, ndipo Satana adzamasulidwa.
Woyipayo adzamemeza anthu ochimwa kuti azinge mzindawo ndi kuuthira nkhondo, koma moto udzatsika kwa Mulungu ndikunyeketsa satana ndi omutsatira ake (Chivumbulutso 20:5,7-9, 14)

Kenako dziko lapansi lidzakonzedwanso mwatsopano (Chivumbulutso 21:1,4), ndipo anthu a Mulungu adzalandira ufumu wosatha. Ichi ndi choonadi cha m’Baibulo chokhudza zaka chikwi—nthawi ya bwinja, chiweruzo, ndi kubwezeretsanso komaliza, osati mwayi wachiwiri kapena ufumu wapadziko lapansi wabwino.

Mpaka Babulo agwe.....





Zukani zukani kwacha tiyeni tikagwire ntchito 🤸🤸🤸🏃🏃🏃🙏🙏🙏Pajatu makolo athu Adamu anachimwa nde ndikuyenera kulima Munda w...
23/04/2026

Zukani zukani kwacha tiyeni tikagwire ntchito 🤸🤸🤸🏃🏃🏃🙏🙏🙏
Pajatu makolo athu Adamu anachimwa nde ndikuyenera kulima Munda wa mphesa Kuti tikhale ndi chakudya🤗🤗🤗🥺🥺
Komanso amapasa olimbika tiyeni tigwire ntchito 🙏🙏🙏


Follow us Jay Marz

Pa chilichonse dalirani mulungu🙏🙏🙏🙏 Osaiwala kupemphera utsiku uno 🙏🙏🙏
22/04/2026

Pa chilichonse dalirani mulungu🙏🙏🙏🙏
Osaiwala kupemphera utsiku uno 🙏🙏🙏

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Jay Marz posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share