Uncle Nodi Online Tv

Uncle Nodi Online Tv Live Streaming, News, Music, Sports, Documentaries and many more

Tsiku linja ndi mawa ukwati wa John ndi Doreen tiyeni tonse tikakumane komko uncle Nodi online tv Ali komko bwelani nons...
02/10/2026

Tsiku linja ndi mawa ukwati wa John ndi Doreen tiyeni tonse tikakumane komko uncle Nodi online tv Ali komko bwelani nonse ku church of Christ masana.

Don't Miss together we can
Let's celebrate together with John and Doreen
Let's help John and Doreen tomorrow

Uncle Nodi online tili komko have a gud night byee.

Breaking News Athu okhala ku chiliampunga akudandaula kwambiri chifukwa Cha athu Ena omwe atseka nseu chifukwa Ali ndi n...
02/10/2026

Breaking News
Athu okhala ku chiliampunga akudandaula kwambiri chifukwa Cha athu Ena omwe atseka nseu chifukwa Ali ndi ndalama ,ndipo athu ayesetsa kudandaulila adindo kuti awathandize kma chilungamo chavuta chifukwa Cha ndalama ,atsogoleri kondani athu Anu omwe akulila,Ife tiyesetsa kukupatsilani ma videos ndi ma Audio omwe Ife tapeza .

Mtandile radio community
Uncle Nodi online
Charity Chipofya

mfumu bwelani poyela kuti tchito yanu idziwike yomwe tinakusankhilani udindo wanu ndipo NDIFE athu okhumudwa kwambiri potitaya chifukwa Cha ndalama.

Together we can.
Let's change our mindset
Let's build Mtandile together
Let's support each other NDIFE AMODZI

Dzuro pa 1/oct/2026 uncle Nodi online tv Gululu ndi senior group piasani 2 ndipo tinakwanitsa kucheza nawo pa interview ...
02/10/2026

Dzuro pa 1/oct/2026 uncle Nodi online tv Gululu ndi senior group piasani 2 ndipo tinakwanitsa kucheza nawo pa interview kma a senior group piasani 2 muli Chingelezi chonveka bwino ndipo anayamba mpaka kumaliza chingelezi chokhachokha ndipo tikamakhala tisamaone ngati mafumu Samantha kuyakhula chingelezi ndipo tikwanitsanso kucheza ndi mafumu osiyanasiyana mu chingelezi kuonetsa chitsanzo chabwino get ready mafumu kumeneko athuwa amakujailani kma mawa ndi a senior group piasani 2 (7:30pm ).

Kma ku Mtandile Mtsiliza Constituency komkoma ndipo tidalandila mdalitso wa zithu zosiyanasiyana kma kukamba za Mbusa uy...
02/10/2026

Kma ku Mtandile Mtsiliza Constituency komkoma ndipo tidalandila mdalitso wa zithu zosiyanasiyana kma kukamba za Mbusa uyu ai ndithu muli pempelo ngati kuti wachita kulemba ndikumawelenga .

Dzuro tonse tinatseka Maso wathu mwa thawi zonse monga tichitila popemphela kma pemphero litayamba ndipo pasanathe mphindi zochepa ambiri anatsekula maso ndikuyamba kusekelela ndi kuvomelela mau omwe mbusayu amenenela pomuuza Mulungu wakumwamba kuti ,Iye pokhala Mulungu wachita mokomela MP Alfred Gangata kuti ndi yemwe adapambana masakho pa 16/Sept/2025 ,ndipo Mulungu amutsogolele pa ulendo wake otsogolela athu okhala mu constituency yake ino.
Panja Pali mau amati pemphero amayakha ndi Mulungu yekha ndiye kuti apa palibe mlandu oyakha pemphero ndi Namalenga basi zikomo powelenga.

Report: Uncle Nodi online

Good morning athu nonse okhala kwa piasan ,Mtsiliza ndi Mwenela kma ngati kuli mzimai olimba mtima komso ochikonda chipa...
02/10/2026

Good morning athu nonse okhala kwa piasan ,Mtsiliza ndi Mwenela kma ngati kuli mzimai olimba mtima komso ochikonda chipani Cha DPP ndi Mai ameneyu ,ndipo salola zopusa amadana ndi katangale amayakhula Live nyo kwa nyo kuthandiza azimai osauka ovutika kuti chilungamo chiyende ngati Madzi,ndipo muli mfundo zabwino monga iye ndi constituency chair lady ndipo amakwanila .

Mai wathu musalole kuti SATANA akusokonezeleni mbiri yanu chifukwa idapita patali chonde tithandizeni athu okhala mu constituency ino kutumikila chipani pamodzi ndi MP Alfred Gangata kmaso Councilor wathu Peter Alex Banda Mai ulemu wanu.

Dzuro azimai ochikonda chipani Cha DPP anasangalala kwambiri ndi mwambo omwe unalipo dzuro pa Mtsiliza school kma ya anavinatu nyimbo zinja za chipani .

Report: Uncle Nodi online

HAPPY BIRTHDAY, HON. ALFRED GANGATAOn behalf of the Central Region Media Team, we wish to extend our warmest and heartfe...
02/10/2026

HAPPY BIRTHDAY, HON. ALFRED GANGATA

On behalf of the Central Region Media Team, we wish to extend our warmest and heartfelt birthday wishes to Hon. Alfred Gangata, Minister of Sports and Vice President for the Central Region.

As you celebrate this special day, we honour your leadership, dedication, and commitment to serving the people. Your role and responsibilities continue to demand wisdom, strength, and determination, and we pray that God grants you abundant grace as you continue with your work.

May this new year of your life bring you good health, renewed strength, wisdom, peace, and greater accomplishments. May God continue to guide your decisions, bless your endeavours, and grant you many more years of meaningful service to the nation and the people of the Central Region.

From all of us in the Central Region Media Team, we wish you a joyous and memorable birthday celebration.

Happy Birthday, Hon. Minister. May God richly bless you and grant you many more years of life and service.

— Central Region Media Team

Lero pa 1/Oct/2026 MP wa Mtandile ndi Mtsiliza Constituency Alfred Gangata  yemwe ndi nduna ya zamasewero ndi chikhalidw...
01/10/2026

Lero pa 1/Oct/2026 MP wa Mtandile ndi Mtsiliza Constituency Alfred Gangata yemwe ndi nduna ya zamasewero ndi chikhalidwe athokonza kwambiri mayor wa mzinda wa Lilongwe kmso ndiyemwe Ali councilor wa Mtsiliza ward pa ntchito yomwe akugwila pa zitukuko za mu mdela lake ndipo MP Alfred Gangata akuti ayesetsa ndi mtima wake kupanga support constituency yake mpaka 2035 ,chifukwa 2030 adzawinanso .

Tsopano ku Mtandile kuli suit ya minister and Mayor ndipo ndi zoona mu mbiri ya chimalawi kuno kukhala ndi mayor kmso minister mu Mtandile Piasan ndi Mtsiliza Constituency.

Uncle Nodi online tv akuthokonza kwambiri a Mayor kmaso aMP Alfred Gangata yemwe ndi MP wadela lino kuti pa Fundo zomwe anayakhula lero ndi fundo zobweletsa UMODZI ndipodi MP uyu waibweletsa pa map Mtandile ndi Mtsiliza Constituency zomwe zili zoona kuti kuno tili Mayor kmaso minister of sports mu mbiri ya dziko kmaso mu mdela la T/A NJEWA kumachenga.
Report: Uncle Nodi online

Athu lero anali osangalala kwambiri ndikufika kwa mphungu wa nyumba ya malamulo Alfred Gangata ndipo athu ambiri anali o...
01/10/2026

Athu lero anali osangalala kwambiri ndikufika kwa mphungu wa nyumba ya malamulo Alfred Gangata ndipo athu ambiri anali okondwa ndikufika kwa MP ameneyu.

Mkulu woyendetsa Ntchito za bungwe la Beautify Malawi Trust Dingiswayo Jere wati khumbo la Mai wa fuko la dziko la Malawi professor Getrude Mutharika, ndikuti ana a sukulu la pulayimale akuphunzira ndikupeza chisamaliro chabwino monga madzi okumwa abwino.

A Jere anena izi lero pa 1st October,2026 ku Mtsiliza Primary school pamene amapereka mphatso ya mpopi wa madzi pa sukuluyi.

Pa nkhani ya Chitetezo pa sukuluyi maka kukonza mpanda umene akuba akugwiritsa ntchito polowera mipata yogumuka, a Jere apempha mfumu ya mzinda wa Lilongwe Peter Banda ndi phungu wa dela la mtsiliza mtandire Constituency. Wolemekezeka Alfred Gangata Komanso mafumu, asukulu komitiyi Kuti akumane ndi kukonza mpandawu.

Mmau ake phungu wa delari wolemekezeka Alfred Gangata athokoza bungwe la Beautify Malawi Trust, mosogoleredwa ndi professor Getrude Mutharika chifukwa Cha masomphenya awo ku Beautify Malawi Komanso kuyankha pempho lawo loti athandize ndi madzi pa sukuluyi.

Bungwe la Beautify Malawi lamanganso zimbuzi ndi manyumba kosinthira atsikana nthawi ya nsambo.

Malingana ndi mphunzitsi wamkulu pa sukulu ya Mtsiliza Primary Mai Chifundo Malange ati sukuluyi mayeso a sitandade 8, ana 99 awasankhira ku sekondale sukulu za Boma ndipo 92% ndi amene akhoza mayeso a sitandade 8 .

Madzi a ukhondowa ati afikanso ku nyumba za aphunzitsi a pa sukuluyi mbali imodzi yochepetsa ma Bill amadzi kunja ku water Board.

Umo ndi mmene ziliri kuno ku Mtandire Mtsiliza constituency ,pa Mtsiliza Primary school.Bungwe la Beautify Malawi Trust ...
01/10/2026

Umo ndi mmene ziliri kuno ku Mtandire Mtsiliza constituency ,pa Mtsiliza Primary school.
Bungwe la Beautify Malawi Trust lero pa 1st October,2026 lapereka chitukuko Cha madzi abwino,aukhondo ku sukulu ya mtsiliza Primary ,kumenenso phungu wa delari ndi wolemekezeka Alfred Gangata, Nduna yoona za masewero, achinyamata ndi chikhalidwe.

Pakalipano mfumu ya mzinda wa Lilongwe wolemekezeka Peter Banda anali komko, a district Governor a Chipani Cha DPP a Lilongwe urban wolemekezeka bambo Christopher Namakhwa analinso komko.

Councilor wadelali Peter Banda wanenetsa kuti aonetsetsa kuti chitetezo chikhale chonkhwima ndipo wachenjeza achinyamata okhala mudela odzugulila mu Mtsiliza Mwenela piasan ndi mwenela kuti pasapezeke okaba zipangizo zomwe zapelekedwa lero .

MP wa kuno Alfred Gangata wati palibenso nkhani yovotanso ndipo inzi zatha pamene milandu yatha dzuro ndipo pano MP wa Mtandile ,piasan ndi Mtsiliza ndi Alfred Gangata palibenso kuchotsela ndipo tonse tiyeni maso pa tsogolo kuti tigwilane manja .

Mafumu ndi ma senor groups anali komko monga momwe mukuonela pa chithuzipo awa ndi a senior group chigoneka anali nawo pa Mwambowu.

* UNCLE NORD ONLINE ✏️

Address

Mtandire
Lilongwe
265

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Uncle Nodi Online Tv posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category