Kuwala

Kuwala This is the official page for kuwalagospelmusic.com

Watch Palibe Music Video by New Jericho CAP Choir Featuring Evance Meleka on the link below
08/07/2025

Watch Palibe Music Video by New Jericho CAP Choir Featuring Evance Meleka on the link below

kuwalagospelmusic.com T/Shirts at K25,000 only ....Tiyankhuleni
04/07/2025

kuwalagospelmusic.com T/Shirts at K25,000 only ....Tiyankhuleni

K25000 Each

🟦 Stream and download Grace Deuka Chirwa songs on kuwalagospelmusic.com
24/06/2025

🟦 Stream and download Grace Deuka Chirwa songs on kuwalagospelmusic.com

🔵 KUWALA SPOTLIGHT 🔵Elizabeth Beatrice Kadyamphungo (LIZBK) anabadwa komanso kukulira ku Zomba kwa a Jokala, Male villag...
23/06/2025

🔵 KUWALA SPOTLIGHT 🔵

Elizabeth Beatrice Kadyamphungo (LIZBK) anabadwa komanso kukulira ku Zomba kwa a Jokala, Male village T/A Malemia. Anabadwa pa 4 April,1982 ndipo mu banja mwawo anabadwa ana 11 ndipo iye ndi wa number 10 (pomwe pakalipano anatsala 7 mubanjali).

Atabadwa anapatsidwa dzina loti Beatrice, ndipo atabatidzidwa, anadalitsidwa ndidzina loti Elizabeth lomwe pachidule ndi Liz, pamene full ili Elizabeth (Liz) Beatrice (B) Kadyamphungo (K)=LizBk.

Mayimbidwe ake anayamba ali wachichepere koma kuimba payekha anayamba 2012 pomwe wakhala akuimba ndi ma Band osiyanasiyana mpaka kuyamba kutulutsa nyimbo zake muchamba cha reggae. LIZBK anayamba kuimbira Ambuye(gospel) muchaka cha 2018 pomwe anatulutsa album yake yotchedwa Khungu.Kuchokera pamenepo wakhala akutulutsa ma album ndi ma singles ake muzamba monga reggae, afro,amapiano ndi zina zosiyanasiyana.LIZBK ndimzimayi wa ana atatu anyamata awiri komanso mtsikana m’modzi.

LIZBK yemwe wadziwika kwambiri ku nyimbo za reggae komanso ndi amapiano ndi nyimbo yoti Wayaka Moto, palibe chida ndi ina yatsopano yotchedwa Nanga kwanuko bwa?LizBk pano adakali ndi project ya nyimbo za praise and worship zomwe zituluke mwezi oyambilira wa 2024.

LIZBK ndimzimayi wa business zosiyanasiyana komanso ndimembala wampingo wa Assemblies of God.LIZBK ndi member wa MUM kwazaka komanso COSOMA.

Address


Opening Hours

Monday 09:00 - 16:00
Tuesday 09:00 - 16:00
Wednesday 09:00 - 16:00
Thursday 09:00 - 16:00
Friday 09:00 - 16:00

Telephone

+265888069117

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kuwala posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Kuwala:

Shortcuts

  • Address
  • Telephone
  • Opening Hours
  • Alerts
  • Contact The Business
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share