Real Friendz

Real Friendz Engage to new Friends, Interacting, Learning new things, Discovering, entertaining.

30/07/2025

Kwanuko akutinji za Mumba?

29/07/2025

JUST IN: Boomplay Southern Africa says it has not paid Zambian Artists on its platform due to low-quality musical content.

Akuti ku Zambia nyimbo zawo sizikhala zothyakuka bwino 😂😅

Zambia Reports

Inu a Mighty Wanderers FC mukungomuwonatu wanuyu akupita sichoncho?  uja wapita basi
28/07/2025

Inu a Mighty Wanderers FC mukungomuwonatu wanuyu akupita sichoncho?

uja wapita basi

Popular American singer, songwriter, and dancer Ciara has officially gained Beninese citizenship after tracing her ances...
28/07/2025

Popular American singer, songwriter, and dancer Ciara has officially gained Beninese citizenship after tracing her ancestry to Benin 🇧🇯

The Grammy-winning artist took a powerful journey to reconnect with her African roots, discovering through DNA testing that a significant part of her heritage links to the West African nation.

- Africa facts

Azathu amene mudapanga za teaching uthenga wanu uwu👇Ntcheu District Council has assured IPTE 14 to 18 aspiring teachers,...
28/07/2025

Azathu amene mudapanga za teaching uthenga wanu uwu👇

Ntcheu District Council has assured IPTE 14 to 18 aspiring teachers, that successful candidates will be selected based on merit.

Principal Human Resources Officer Elias Kawuwa made the remarks at the end of the interviews, conducted at the district's stadium.

Kawuwa said the council will collaborate with the Anti-Corruption Bureau (ACB) and other stakeholders to select successful teachers, who will start work in September this year.

He expressed hope that the 850 teachers to be employed will help alleviate teacher shortages in the district.

One interviewee, Ballos Chacy Kamenya, expressed hope for employment, citing his 2014 training.

The government plans to employ around 26,000 aspiring teachers nationwide who completed their studies between 2014 and 2018.

Kuno ndie talawilira kulangizidwaHEKEN 👇
28/07/2025

Kuno ndie talawilira kulangizidwa
HEKEN 👇

Nyimbo ikukamba zoti tizikhala bwino ndi athu kupangira pa mawa othandiza mzake sadziwika.

The Jaki Show usatitutumutsetu 😂🙌👇Chinthu chowoneka ngati mwala chinawoneka mlengalenga.A Science akuchitcha '3I/ATLAS'....
28/07/2025

The Jaki Show usatitutumutsetu 😂🙌
👇
Chinthu chowoneka ngati mwala chinawoneka mlengalenga.
A Science akuchitcha '3I/ATLAS'.

Komwe chinachokera nkosadziwika.
Ma Scientist ena anena kuti akukhulupilira kuti ndi technology ya ma Alien ndipo chikuzungulira mu solar system.

Ma scientist akuti akuganiza kuti chinthuchi chikupanga study za mu earth ndipo mu November, chidzakhala chitabisika ndi dzuwa.

Pamenepo chikhoza kudzapanga attack earth. Anena ndi a daily record.

ANOTHER ONE.Wina apwetekedwaso apa
28/07/2025

ANOTHER ONE.

Wina apwetekedwaso apa

Today's Results
27/07/2025

Today's Results

Akuti lero kunali game koma fixture kutsogoloku sidasintheko kanthu.
27/07/2025

Akuti lero kunali game koma fixture kutsogoloku sidasintheko kanthu.

27/07/2025

Kodi game ya Bullets yukutha bwanji?

27/07/2025

Komasotu kusiyana kuja kudapangitsa kupeza alamwanu enieni
Ndipo ndie akundisamala
😅😅

Address

Devil Street
Lilongwe
[email protected]

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Real Friendz posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share