MBriefs

MBriefs π–Έπ—ˆπ—Žπ—‹ 𝗉𝗋𝖾𝗆𝗂𝖾𝗋 π—Œπ—ˆπ—Žπ—‹π–Όπ–Ύ π–Ώπ—ˆπ—‹ π–Όπ—ˆπ—‡π–Όπ—‚π—Œπ–Ύ, 𝗍𝗂𝗆𝖾𝗅𝗒 bite-sized briefs π–Ώπ—‹π—ˆπ—† 𝖬𝖺𝗅𝖺𝗐𝗂 𝖺𝗇𝖽 π–»π–Ύπ—’π—ˆπ—‡π–½. π–₯π—ˆπ—…π—…π—ˆπ— π—Žπ—Œ π–Ώπ—ˆπ—‹ 𝗍𝗁𝖾 π—…π–Ίπ—π–Ύπ—Œπ— π—‡π–Ύπ—π—Œ, π—π—‹π–Ύπ—‡π–½π—Œ, 𝖺𝗇𝖽 π—‚π—‡π—Œπ—‚π—€π—π—π—Œ! We are π–¬π–‘π—‹π—‚π–Ύπ–Ώπ—Œ!
(1)

15/09/2025
Justice Dr Jane Ansah lero anakafika pamalo pamene panagwera ndege imene inapha Saulos Chilima ndi anthu ena.
19/08/2025

Justice Dr Jane Ansah lero anakafika pamalo pamene panagwera ndege imene inapha Saulos Chilima ndi anthu ena.

β€’Blantyre's Chileka International Airport is now Bakili Muluzi International Airportβ€’Lilongwe's Area 18 Interchange is n...
19/08/2025

β€’Blantyre's Chileka International Airport is now Bakili Muluzi International Airport
β€’Lilongwe's Area 18 Interchange is now Arthur Peter Mutharika Interchange
β€’Lilongwe Western Bypass Road is now called Joyce Banda Highway.

The changes follow a presidential directive on Monday, 18 August 2025.

16/08/2025

Map a kwa Nepman ... πŸ€”πŸ’­πŸ‘€

Mfumu yaikulu Kachindamoto ya ku Dedza yamwalira lero pa Chipatala chachikulu cha Kamuzu Central ku Lilongwe. Mmeneri wa...
13/08/2025

Mfumu yaikulu Kachindamoto ya ku Dedza yamwalira lero pa Chipatala chachikulu cha Kamuzu Central ku Lilongwe.

Mmeneri wa unduna wa maboma aang'ono a Anjoya Mwanza atsimikiza za nkhaniyi.

Mzimu wawo uwuse mumtendere.

MP wawina chisankhoBungwe la MEC lalengeza kuti Lawrence Maziya wa MCP ndiye akhale phungu wa nyumba ya malamulo kuimira...
12/08/2025

MP wawina chisankho
Bungwe la MEC lalengeza kuti Lawrence Maziya wa MCP ndiye akhale phungu wa nyumba ya malamulo kuimira Lilongwe Chilobwe constituency. Izi zabwera chifukwa ku derali kunalibe wina WA chipani chilichonse kapena wa independent amene anaonetsa chidwi choimira.

Mα΄€ΚŸα΄€α΄‘Ιͺ's κœ°α΄œα΄‡ΚŸ α΄„Κ€ΙͺsΙͺs κœ°α΄€Κ€ κœ°Κ€α΄α΄ ᴏᴠᴇʀ. Essential as fuel is to the economy of Malawi, one would expect a robust supply chai...
11/08/2025

Mα΄€ΚŸα΄€α΄‘Ιͺ's κœ°α΄œα΄‡ΚŸ α΄„Κ€ΙͺsΙͺs κœ°α΄€Κ€ κœ°Κ€α΄α΄ ᴏᴠᴇʀ.

Essential as fuel is to the economy of Malawi, one would expect a robust supply chain to ensure steady supply. However, the procurement of the commodity appears to be one of the most lucrative sections of government. Deals made behind locked doors to favor individuals, numerous administrative loop-holes, mismanagement, political interference, deliberate cover-ups, and widespread corruption are characterist of the fuel supply chain in Malawi. If we fail to address the real issues affecting the fuel supply into the country, we should expect a much deeper crisis with far reaching implications. Prudence, integrity, accountability... for the people, for the country, let us all work for a better nation and not prioritize personal interest.

Lero, president Chakwera wachita nawo mapemphero ku mpingo wa African ku Karonga. Pa mapempherowa, Dr Lazarus Chakwera a...
10/08/2025

Lero, president Chakwera wachita nawo mapemphero ku mpingo wa African ku Karonga.

Pa mapempherowa, Dr Lazarus Chakwera awerenga mau a mu buku lopatulika ochokera pa Luka 1 verse 1 mpaka 5.

President Dr  Lazarus Chakwera is today attending the 2025 Umuthetho Cultural ceremony at the Hora Heritage Centre in Mz...
09/08/2025

President Dr Lazarus Chakwera is today attending the 2025 Umuthetho Cultural ceremony at the Hora Heritage Centre in Mzimba under the theme "Cultural Diversity, the foundation for Peaceful Co-existence and Development."

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MBriefs posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to MBriefs:

Share