Malawi Light

Malawi Light Educating, Entertaining and Informing

02/11/2023

Police in Lilongwe have arrested seven suspected armed robbers who are suspected to be involved in killings and robberies in Lilongwe.

National Police spokesperson Peter Kalaya said that the suspects are connected to five criminal cases, including the murder of a Chinese national at Njewa and the stealing of K35 million in Lilongwe's Area 3.

He said: "We found these people with two vehicles, an AK-47 and a pistol which they were using. So far, their arrest has helped us to solve five criminal cases which the police have been following up."

Kalaya further explained that these suspected criminals were operating from Mangochi but had Lilongwe-based operatives as possible target identifiers for their criminal operations.

The suspects are six men and one woman. The Police have identified the suspects as; Mussah Austine (50), Tailosi Mkwapatila (44), Yamikani Alderico Petro (42), Muhammad Jamali (41), Yusufu Adam (40), Blessings James (34), and Precious Biliat (31). Kalaya further said that these suspects have been targeting Chinese nationals.

Light

01/11/2023

M'dziko la Spain, a Fernando Fitz-James Stuart awaletsa kuti asatchule mwana wawo wamkazi amene wabadwa masiku asanu apitawa chifukwa dzinalo latalika kwambiri. Malinga ndi Sky News, a 'duke' amenewa awakaniza kutchula mwanayo dzina loti Sofia Fernanda Dolores Cayetana Teresa Angela de la Cruz Micaela del Santisimo Sacramento del Perpetuo Socorro de la Santisima Trinidad y de Todos Los Santos.
Komatu zina Ukamva........

30/10/2023

Bwalo la milandu ku Phalombe latulutsa pa belo Joe Gwaladi amene adamumanga sabata yatha pomuganizira kuti adavulaza mkazi wake F***y Khuliwa wa zaka 22.

Majisitileti Leonard Mtosa walamula kuti Gwaladi asapezekenso ndi mlandu wozunza kapena kumenya mkazi wakeyo ndipo akatero beloyo idzathetsedwa choncho adzalowanso m’chitokosi.

Apa bwalolo lidalamula Gwaladi kuti apereke chikole cha K200 000 komanso ndalama zokwana K50 000. Woimbayo, yemwe amadziwikanso kuti mwana wa ku Mulomba, adamangidwa Lachiwiri sabata yatha pomuganizira kuti adamenya ndi kuluma chala cha mkazi wakeyo.

Zonse n’chabe, a Mtosa apereka beloyo Khuliwa ku m’mawaku atapempha bwalolo kuti liutaye mlanduwu. Koma iwo adati mphamvu yothetsa mlanduwo lili m’manja mwa boma.

Woimira boma pa milandu a Dingiswayo Mbepula adati mlanduwo akhoza kuutaya ngati mbali ziwiri za banjalo zitamvana zoti apolisi authetse.

“Zimene akambirane ndizo titsate kuti mlanduwo uthetsedwe kapena tipitirize kuuzenga,” adatero a Mbepula.

Zomwe mbali ziwirizo zimvane zidzamveka m’bwalolo Lolemba likudzali.

24/10/2023

Katswiri oimba nyimbo m'dziko muno Joe Gwaladi ali m'manja mwa apolisi atamangidwa pa mlandu omuganizira kuti wamenya ndi kuvulaza mkazi wake.

Izi zinachitika pamalo ochitila malonda a Mulomba Trading ku Phalombe usiku wapitawu.

Mneneri wa polisi ya Phalombe a Jimmy Kapanja watsimikiza zakumangidwa kwa Gwaladi.

Apolisi ati akufufuzabe za nkhaniyi.

Light

Address

Lilongwe

Telephone

+265888443675

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Light posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Malawi Light:

Share

Category