06/04/2026
Mtsikana mukumuona apatu dzina lake ndi charity foliano wa boma LA balaka pa liwonde roadblock mtsikanayu wapezeka atafa mdera Lina lotchedwa mawira ma report akusonyeza kuti charity foliano wasowa Saturday ndipo wapezeka lelo ataphedwa mmmmm amalawi azanga kunjaku kwavuta tiyeni tigwilane manja pothana ndizigawenga kms osakhulupilila ma calls achilendo pa 4n yanu mulungu akudaliseni ndipo osawaila kutipanga folo pano kuti zambili zisakuphonyeni