Itz Mmie

Itz Mmie We listen we dont judge 🙌🦾

From the winning team 🔥. Tili bwinobwino ndipo sitik*tekeseka. Boma ndi la Laz ili.
22/09/2025

From the winning team 🔥. Tili bwinobwino ndipo sitik*tekeseka.
Boma ndi la Laz ili.

Tsogolo lathu lili mmanja mwa Chakwera
20/09/2025

Tsogolo lathu lili mmanja mwa Chakwera

20/09/2025

Dan Lu zoona mwatituluka kale nthawi yomweyi? Ife timalimba ntimatu 😪. Komanso ndisakunyengelele utha kumapita kwa agogowo MCP sinatenge boma chifukwa chaiwe..

BOMA NDILOMWELI BAS!!!

Biggy with  only 5 districts (Lilongwe, Dowa,Dedza and Mchinji and Rumphi  ali kale ndi 1,250,000 votes k*t tikwqnise 50...
20/09/2025

Biggy with only 5 districts (Lilongwe, Dowa,Dedza and Mchinji and Rumphi ali kale ndi 1,250,000 votes
k*t tikwqnise 50+1" (2,200,000) we just need 950,000 votes

750,000 votes tipeza in these districts

1.Ntchisi
2.kasungu
3.Salima
4.Nkhotakora
5.Mzimba
6.Nkhata bay
7.Karonga

200,000 tipeza motere
1.The entire southern region kuli athu 360,000 votes

2.Chitipa and Likoma we have 21,000

Dont worry my president Dr Lazarus Chakwera boma sililupita kulikonse 🔥🔥🔥

Ndipo nde zikudabwitsa kaya nde mukumakwiya chani?!!Mukhaula simunati
20/09/2025

Ndipo nde zikudabwitsa kaya nde mukumakwiya chani?!!

Mukhaula simunati

Ndipo DPP CAN NEVER, I repeat can never win this elections Dr Lazarus Chakwera ak*tenga BamaEnanu mudyatu ntolilowo simu...
20/09/2025

Ndipo DPP CAN NEVER, I repeat can never win this elections

Dr Lazarus Chakwera ak*tenga Bama

Enanu mudyatu ntolilowo simunati

Chili mweee akuchita kudziwa k*ti game ili mbali yake.Dr Lazarus Chakwera ndi dolo kwambiri enanu muinvera fungotu
20/09/2025

Chili mweee akuchita kudziwa k*ti game ili mbali yake.
Dr Lazarus Chakwera ndi dolo kwambiri enanu muinvera fungotu

Amene akukhulupilila izizi amatamba. MEC ndiyomwe ikunena zonse osati zopusazo. Nde inu a DPP busy kusangalala ndima das...
20/09/2025

Amene akukhulupilila izizi amatamba. MEC ndiyomwe ikunena zonse osati zopusazo. Nde inu a DPP busy kusangalala ndima dashboard ngati awa. Mupepela nazo izi. Ndipo mudzidzimuka once DR LAZ atakhalaso President another five years.

Tamapangani phokoso lanu lopanda ntchito lo.

20/09/2025

Tikunenatu k*ti boma ndilomweli, m***a kumanamizana ndima results a unofficial wo. Koma boma ili tik*tengaso mpaka 2030 woooooooo!!!!!!

Komanso uyuyu tinasankha tokha sizingatheke k*ti boma liluze ndipo mwauponda. You will be surprised akunena k*ti MCP yat...
20/09/2025

Komanso uyuyu tinasankha tokha sizingatheke k*ti boma liluze ndipo mwauponda.
You will be surprised akunena k*ti MCP yatengaso boma just watch!!!!

Game ndiya wadya mtolilo iyi.

Chi team ichichi chivulaza matimu. Palibeso kubwerela boma tik*tengaso ili, chitukuko tipitilize.Opposition ndiyomweyo a...
20/09/2025

Chi team ichichi chivulaza matimu. Palibeso kubwerela boma tik*tengaso ili, chitukuko tipitilize.

Opposition ndiyomweyo and boma ndilomweliso. Like it or not !!!

Address

Lilongwe

Telephone

+265885960698

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Itz Mmie posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Itz Mmie:

Share