Today's Press Online

Today's Press Online Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Today's Press Online, Media/News Company, Lilongwe.

Zikomo Yesu.
10/03/2025

Zikomo Yesu.

MWANA WA MKAYA AKULUTIZGA KUGWILA NTCHITO YIWEMI MU MZIMBA WEST CONSTITUENCYPa 16 February 2025 wakhazikiska ntchito yak...
18/02/2025

MWANA WA MKAYA AKULUTIZGA KUGWILA NTCHITO YIWEMI MU MZIMBA WEST CONSTITUENCY

Pa 16 February 2025 wakhazikiska ntchito yakupereka chakurya ku ŵachekulu. ŵamoza mwa ma agho ŵaphindula kale nantchito iyi mba Gogo Mr na Mrs Tchakisi ku Thunduwike pasi pa GVH Jojojo Mkandaŵire, awo ŵapokera thumba la ngoma nama gulosalezi.

Mu mazgo ghakhe Kumwenda watisimikizgila kulutizga na ntchito yakufikila awo mbakusuzgikilapo. Apa nkhachiŵiri kulondezga ntchito yantheura ya mu 2024.

Aeckim wazamwimilira dela la Mzimba West ngati Independent MP pa 16 Seputemba 2025.

Aeckim Kumwenda ntchisola cha ŵanandi mu Vigawa nga Malidade, Manolo, Moliya, Mpherembe, Tchesamu, Kazuni, na ghanandi. ✅✅✅

✍🏿Fredrick Ausman Chaula
📸In picture: Aeckim Kumwenda na Gogo NyaMhango (Mrs Tchakisi)

Eli Njuchi Waiphula. Congratulations to you bro 💯
29/01/2025

Eli Njuchi Waiphula. Congratulations to you bro 💯

29/01/2025

Big shout out to our newest top fans! Chimwemwe Maclawrence, Za Mawa, Brave Nyasulu, Fredrick Asosoli Ndege
Thanks for being part of us. We are here because of you guys. God bless you all 🙏

Amene adayika ichichi panja ngati apa amkaganiza chani kwenikweni? 😅 Iyi ndi nyumba yachifumu ndipo imayenera ikhale pam...
29/01/2025

Amene adayika ichichi panja ngati apa amkaganiza chani kwenikweni? 😅 Iyi ndi nyumba yachifumu ndipo imayenera ikhale pamalo abwino okuti wina asakusokoneze ayi 😃.

Uyu apweteka gulu. People are jobless now chifukwa cha ziganizo zawo bwanawa. Makamaka pama ARV pokhapa apa ambiri tipwe...
29/01/2025

Uyu apweteka gulu. People are jobless now chifukwa cha ziganizo zawo bwanawa. Makamaka pama ARV pokhapa apa ambiri tipwetekeka 😪.

29/01/2025

January akupita kumapeto uyu azibambo bwererani kunyumba please 😃

UEFA CHAMPIONS LEAGUE WEEK 818 games in one night Tiyiikunge motani ticket ya lero apa? Ma game onse akuyamba nthawi yof...
29/01/2025

UEFA CHAMPIONS LEAGUE WEEK 8

18 games in one night

Tiyiikunge motani ticket ya lero apa? Ma game onse akuyamba nthawi yofanana usiku uno.

28/01/2025

TODAYS PRESS ONLINE: DISO LANU.

Mwaswera bwanji ah Malawi kuli konse komwe muli? Timakunyadirani kwambiri. Dziwani kuti page li lilipo. Tinali busy kukoza zina ndi zina kuti tizikufikirani mwaukadaulo ndiponso mwandondomeko. Dziwani kuti ma admin anu akutakataka zinthu zingapo kuti tsamba lino likhare lotsogora.

lanu.

24/01/2025

Awuzeni anzanuwo kuti kwacha ndinthawi yothamangitsa ma hustle. Nyengo isakupusitseni.

Good Morning

24/01/2025

Big shout out to my newest top fans! Chimwemwe Maclawrence, Gelsom Zamawa, Brave Nyasulu, Fredrick Asosoli Ndege

Breaking News Michael Usi wathamangitsidwa mu chipani cha UTM ati kamba kobweretsa chitsokonezo
30/12/2024

Breaking News

Michael Usi wathamangitsidwa mu chipani cha UTM ati kamba kobweretsa chitsokonezo

Address

Lilongwe

Telephone

+265997163170

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Today's Press Online posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share