Suleman Atupele Chitera

  • Home
  • Suleman Atupele Chitera

Suleman Atupele Chitera Malawi youth political activist Together we can make abetter malawi
(1)

Kenya's President William Ruto has ordered police to shoot in the legs protesters targeting businesses.Kenyans have from...
10/07/2025

Kenya's President William Ruto has ordered police to shoot in the legs protesters targeting businesses.

Kenyans have from Monday this week been protesting against police brutality, among other reasons.

Ruto says those targeting shops should be incapacitated but not killed.

"Anyone caught burning another person's business or property should be shot in the leg, hospitalized, and later taken to court. Don't kill them, but ensure their legs are broken," the president said.

Meanwhile, United Nations and human rights groups have accused the police of using excessive force in the recent wave of anti-government protests.

-BBC-

09/07/2025
📢 **Send Us Your Stories for Publication!** Have a story to share? **Reach over one million readers** by publishing with...
09/07/2025

📢 **Send Us Your Stories for Publication!**

Have a story to share? **Reach over one million readers** by publishing with us. Whether it's news, opinion, or community updates — your voice matters.

📩 **Submit now and be heard!**

Bungwe la MEC lati, chiwerengero cha anthu omwe atenga kalata zowavomereza kuyima nawo pa chisankho chikudzachi pa mpand...
09/07/2025

Bungwe la MEC lati, chiwerengero cha anthu omwe atenga kalata zowavomereza kuyima nawo pa chisankho chikudzachi pa mpando wa mtsogoleri wa dziko chinakali pa 15.

M'neneri wa bungweli a Sangwani Mwafuriwa wati, tsiku loti anthu omwe akuyima nawo pa chisankhochi ayambe kupereka zikalatazi ku MEC ndi pa 24 July kufika pa 30 July.

Iwo atinso pa 14 July ndi pomwe atsekulire movomerezeka kuti anthu atha kuyamba kuchita misonkhano yokopa anthu kuti adzawavotere.

MEC yatolera 150 miliyoni kwacha kwa atsogoleri 15 wa, komanso ndalama za nkhani nkhani kwa omwe akuyimira ngati a phungu ndi ma khansala mdziko muno.

08/07/2025

ATUPELE MULUZI WATI, MCP ICHOKE KUTI ZINTHU ZISINTHE.

ATUPELE WATI , AMALAWI AKUFUNA KUTI IYEYO AWAMENYELE NKHONDO PAMODZI NDI ZIPANI ZINA KUTI ACHOTSE MCP.

ATUPELE WALONJEZA KUTI NKHONDO YOCHOTSA MCP AYIGWIRA KUTI AMALAWI AONE KUSINTHA.

ATUPELE WATI, AKUONA NDIPO AKUZINDIKIRA KUTI ZINTHU SIZILI BWINO CHIFUKWA CHA MCP.

Address


Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Suleman Atupele Chitera posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Suleman Atupele Chitera:

Shortcuts

  • Address
  • Alerts
  • Contact The Business
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share