Best in jingle production, radio and tv programming ,Product awareness campaigns and many more
24/07/2025
Police yaitanitsa mtsikana otchuka ndi dzina loti ‘Small Wifey’ kuti loweluka ikamati 10am akaonekele ku Police FM kumene kuli interview. Police FM ikufuna Itadziwa Luso limene Small Wifey ali nalo
24/07/2025
Ambili akugona 😎
Catch small wife on Police FM via 92.4MHz on Saturday.
My inbox is open for all up & coming artist. Lets promote your music / brand
Models
Artists
Writers
Poets
Dancers
Hustlers
Actors
This programm is for you. Hit my inbox or WhatsApp 0998340295
Terms and conditions Apply 👌
02/07/2025
Anena anena
Azafotokoze bwinobwino...
12/01/2025
Tiyeni tikhalile limodzi pa Police FM Radio kuyambila pano mpaka 8 koloko madzulo ano.
92.4MHz tatsekulani wailers yanu.
Tasankhani nyimbo imodzi ku comment section ku yoti ndikuseweleleni.
08/01/2025
Tiyambe chonchi chakachi bwa?
Loweluka ndikhala ndikucheza ndi Grandie Gbung Simbungi mu program yotchedwa pa Police Fm Radio.
Mukhoza kudzamvela pa 92.4Mhz kapena 92.6Mhz.
Kwa ma onse amene akufuna kupeza mwai wa interview pa Police Fm Radio, Timvane pa 0882430605 wap.
03/12/2024
It's EP pa 22 December.
Zambili zili pa posta po ndipo ma artist a ku Lilongwe ndimadela ena onse ozungulila talembesani pa 0882430605 .
23/11/2024
Full time silver 0-0 bullets
George Chikooka voted man of the match
23/11/2024
Silver vs Bullets
33 minutes, corner fpr silver strikers, Uchizi Vunga to take the corner and the ball goes straight into palms of Bullets goalkeeper.
Be the first to know and let us send you an email when Dj Young Teacher posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.