
13/04/2025
Kwa omwe muli ndi ma sisters Anu Kodi amakupangani support pa zomwe mumapanga ? lero tiyeni timphuzire Ku Chokera Kwa ma sister a Kell Kay. Instead kuti Kell Kay Ku mauza ma model kuti azimu bakira nyimbo zake ma twin sisters Ake anangodzipereka basi kuti achimwene musadandaule ifeyo tilipo tizikuvokerani inu pa easy. Pano a Kell Kay ndi adolo chifukwa chathandizo la ma sisters awo. Inuso yambani kukondana ndi ma sisters Anu
Lero Kambwiri sisters akukumbukira tsiku lomwe anabadwa KUCHOKERA kuno ku Artist Wathu tikuti Happy Birthday ma sisters ππππππ