MTsukuluzi 265

MTsukuluzi 265 The Malawian page full of Social media influencers, content creators, public figure🥇🎖️

LET'S LIKE/FOLLOW.. Verified󱢏
(1)

Follow MTsukuluzi 265🤣MA buddy avutawa🙏😋🙌
18/07/2025

Follow MTsukuluzi 265
🤣MA buddy avutawa🙏😋🙌

Follow MTsukuluzi 265Kod mukuti kwagwanji ndi celleb wanuyi😥😋
18/07/2025

Follow MTsukuluzi 265
Kod mukuti kwagwanji ndi celleb wanuyi😥😋

Follow MTsukuluzi 265Tiyeni tiathandize kusangalala birthday adad (prod. Auther Peter wamuthalika) 🎂
18/07/2025

Follow MTsukuluzi 265
Tiyeni tiathandize kusangalala birthday adad (prod. Auther Peter wamuthalika) 🎂

Follow MTsukuluzi 265Nde Pali ma phone ena amakuonesa ngat mungelo 😂😂Mwaswebwanji ndi itel?
18/07/2025

Follow MTsukuluzi 265
Nde Pali ma phone ena amakuonesa ngat mungelo

😂😂
Mwaswebwanji ndi itel?

Follow MTsukuluzi 265Anthu simukuyankhula bwino, munthu asadye Nsima ngati mpunga sakuufuna
18/07/2025

Follow MTsukuluzi 265
Anthu simukuyankhula bwino, munthu asadye Nsima ngati mpunga sakuufuna

Follow MTsukuluzi 265Chisankho ndi mtima wanuMen ...Left, Centre or Right?🤔
18/07/2025

Follow MTsukuluzi 265
Chisankho ndi mtima wanu
Men ...Left, Centre or Right?🤔

Follow MTsukuluzi 265Anthu mukuyankhulisa polani moto😁😋
17/07/2025

Follow MTsukuluzi 265
Anthu mukuyankhulisa polani moto😁😋

Follow MTsukuluzi 265Ameneyu ndi amene wapangitsa kuti ma presentation kuno akhale a m’Chichewa. Koyambilira amangoti “Y...
17/07/2025

Follow MTsukuluzi 265

Ameneyu ndi amene wapangitsa kuti ma presentation kuno akhale a m’Chichewa. Koyambilira amangoti “Yeah, yeah, yeah” mpamene anthu anazindikira kuti zambiri zikumudutsa.

📸 MTsukuluzi 265

17/07/2025

Kupanga chibwezi Bola kudya Mbewa zothila nsinjiro😋😁

Follow MTsukuluzi 265Kod mwati Zukhala bwanji mmakukamu🤣🙏
17/07/2025

Follow MTsukuluzi 265
Kod mwati Zukhala bwanji mmakukamu🤣🙏

Follow MTsukuluzi 265Morale the rapper waoneka2 bwino relo osati zake zija zomangotionesa ma tattoos ake otukwana aja🙏
17/07/2025

Follow MTsukuluzi 265
Morale the rapper waoneka2 bwino relo osati zake zija zomangotionesa ma tattoos ake otukwana aja🙏

Follow MTsukuluzi 265Musamakhale ndi phuma mukamajambulisa nanga azanu sangatupe phazi ndi chiphwanya nchengacho😥
17/07/2025

Follow MTsukuluzi 265
Musamakhale ndi phuma mukamajambulisa nanga azanu sangatupe phazi ndi chiphwanya nchengacho😥

Address

Salima

Telephone

+265880614970

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MTsukuluzi 265 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to MTsukuluzi 265:

Share