Follow The God's steps

Follow The God's steps Follow the God's steps, it is a page specifically for good message of God.
(1)

It is there to inspire the ages, that there is no one else throughout the universe to serve if not God Almighty.

29/03/2025
29/03/2025
29/03/2025

Yehova akayimilira pamoyo wako zazikulu zimachitika.Ofuna kupangidwa add ku WhatsApp group ikani no yanu.

29/03/2025

MPEMPHERO LA UTSIKU PA 29/03/25.

ATATE MBUYE WATHU YESU KHRISTU TAGWADA PAMASO PANU KULAMBIRA DZINA LANU LAMPHAMVU LIMENE LODZADZA NDI ULEMELERO NTHAWI ZONSE , PAMENE TAFIKA PA MASO PANU TIKHULULUKIRENI ZOCHIMWA ZATHU.

PAMILOMO YATHU CHOYAMBA KUTHOKONZA CHISAMALIRO CHANU KUCHOKERA MAWA UJA PAKA PANO ZIKOMO KWAMBIRI.
USIKU WAGWA TISOWA INUYO MUKHALE PAKATI PATHU KUTITEZA KU ZOLUSA ZA KUMIDIMA ZIMENE SIZISAGALALA NDI MIYOYO YATHU.
MPHAMVU YA MZIMU OYERA IKHALE NAFE NGATI TSIKU LA PETEKOSITI LIJA.

LERO KULIBE KUPEMPHA ZAMBIRI KWATHU KUTHOKONZA KWAMBIRI PA MADALITSO ONSE AMENE MWAPEREKA KWA IFE ZIKOMO KWAMBIRI.
OSAIWALA MUKAWACHIRITSE ODWALA MWA YESU KHRISTU AMEN.

Kumakhala chimwene kumwamba pamene munthu watembenuka ntima. AMEN πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™
24/03/2025

Kumakhala chimwene kumwamba pamene munthu watembenuka ntima.

AMEN πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™

24/03/2025

With Baibulo Langa Moyo Wanga – I'm on a streak! I've been a top fan for 5 months in a row. πŸŽ‰

24/03/2025

With Vumbulutso Langa – I just got recognized as one of their top fans!

22/03/2025

Nkhope ya MULUNGU iwalire moyo wanu Lero. Mukhale m,gonjetsi pa CHILICHONSEπŸ™‹πŸ‡²πŸ‡ΌπŸŒ

22/03/2025

MPHUNZIRANI CHIKONDI CHENI CHENI KUCHOKERA KWA YESU KHRISTU..

MUNTHU AKATI KUTI NDIKONDA MULUNGU NA DANA NAYE BALE WAKE ALI WA BODZA , PAKUTI IYE OSAKONDA BALE WAKE AMENE WAMUONA,SAKHONZA KUKONDA MULUNGU AMENE SAMUONA. NDIPO LAMULO ILI TILI NALO LOCHOKERA KWA IYE KUTI IYE AMENE AKONDA MULUNGU AKONDENSO BALE WAKE .YOHANE 4:20-21.

NGATI MULIBE CHIKONDI MUPEMPHE YESU KHRISTU AKUPATSENI CHIKONDI.
ABALE ANU KUMAVUTIKA KOMA INUYO MULIKUTHEKERA KUTI MUKHONZA KUTHANDIZA CHIKONDI MULIBE.

CHAKUDYA MULINACHO CHAMBIRI KOMA NEBA KUMAGONA NDI NJALA OSAPATSAKO CHIKONDI MULIBE.

NDALAMA MULINAYO KOMA KUKANIKA KUBWEREKA ZANU CHIKONDI MULIBE.

PHUNZIRANI CHIKONDI CHA MULUNGU AMENE AMAVUMBITSA MVULA KWA OCHIMWA NDI OLUGAMA .
AMAPEREKA MOYO KWA OCHIMWA KAPENA OLUGAMA.
CHIKONDI CHISAPANGE NSAKHO UKONDE ALIYENSE CHIMODZI MODZI.

MTENDERE WA AMBUYE WATHU YESU KHRISTU UKHALE NANU PAMENE TIKUPHUZIRA CHIKONDI CHENI CHENI KUCHOKA KWA YESU KHRISTU.
LAPANI MATCHIMO MUKHALE FULU MWA YESU KHRISTU.

Address

Lilongwe

Telephone

+265885811868

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Follow The God's steps posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share