Shasha pamalawi

Shasha pamalawi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Shasha pamalawi, Digital creator, Lilongwe.

20/08/2024
Vacation star, JB ready to drop another hit today 🎶Ndinyimbo itii yomwe imakusangalatsa yabwanawa ?? Osaiwala kupanga li...
19/04/2024

Vacation star, JB ready to drop another hit today 🎶

Ndinyimbo itii yomwe imakusangalatsa yabwanawa ??

Osaiwala kupanga like this page

Confirmed :-  Queen Sheba akubwela kudzakhazikika ku Malawi September ameneyu pamene akuyamba campaign ya mpando wau M.P...
19/04/2024

Confirmed :- Queen Sheba akubwela kudzakhazikika ku Malawi September ameneyu pamene akuyamba campaign ya mpando wau M.P.

Iyeyu akudzayimila ngati independent M.P ku Lunzu mu 2025 moti alipa ndia Shado
Mawu Anu ndiotani kwaashado

Follow page imeneyi madzulo ano 7 o'clock tikhala tikugawa credit thanks

Sad:- Zachitika pompano chapa Kanjedza Assemblies. Minibus yo kaya inaluza ma break nkuphonya nseu kugwa nkugundanso mun...
17/04/2024

Sad:- Zachitika pompano chapa Kanjedza Assemblies. Minibus yo kaya inaluza ma break nkuphonya nseu kugwa nkugundanso munthu amene wamwalila pompo.

Anthu adali mu minibus mo avulala

Lelo gululu ndimamuna aligoneUyu ndi shasha Pamalawi mawu amodzi kwaiyee.
17/04/2024

Lelo gululu ndimamuna aligone
Uyu ndi shasha Pamalawi mawu amodzi kwaiyee.

Ma shasha odzitsataa
17/04/2024

Ma shasha odzitsataa

Compensation ipose apa 🤣🤣😂😘Follow shasha pamalawi
17/04/2024

Compensation ipose apa 🤣🤣😂😘
Follow shasha pamalawi

Shasha wanu uyu ndi Pick Poh. Ameneyu ndimnyamata wadzaka 24 ndipo tinganene kuti ndi half cast tunena izii Malingana nd...
17/04/2024

Shasha wanu uyu ndi Pick Poh. Ameneyu ndimnyamata wadzaka 24 ndipo tinganene kuti ndi half cast tunena izii Malingana ndimaonekedwe ake okopa anyway tamupangeni follow mwanayi mmenemu muli luso kwambi ndipo mayimbidwe ake ndiokoma kwambili mwanyimbo zomwe anaimba ndipo zopatsa mudyo ndi izii

1:Nane
2:Cant be again
3:Nacho
4:Pholoso ft Silence Platinumz
5:Tsoo
6:Wappa ft
7:Yalu ft Tammie
8:Monalisa
9:I don't fear like momy
Etcc.......
Mwa shasha ameneyu simuzakhumudwa
Follow shasha pamalawi

Kodi ndi angat akuidziwa nyimbo iyii!??Like Shasha pamalawi
17/04/2024

Kodi ndi angat akuidziwa nyimbo iyii!??

Like Shasha pamalawi

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Shasha pamalawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share