Pabwalo

Pabwalo Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Pabwalo, Digital creator, Area 49, Street 2, Lilongwe.

Grandie Gbung Simbungi wati ali okonzeka kutulutsa Extended playlist ija chidule inatchedwa kuti EP. Iye wati mwambo ons...
03/12/2024

Grandie Gbung Simbungi wati ali okonzeka kutulutsa Extended playlist ija chidule inatchedwa kuti EP.
Iye wati mwambo onse uzachitika pa 22 December 2024 ku lilongwe ku area 18 C kumalo otchedwa Las Vegas ena amangoti ku Nankhaka.

Iye was wauza Pabwalo kuti Ep imeneyi ili ndi nyimbo 6 ndipo akuigulisa pamtengo osachepela MK 10 000 yokha basi.
Ma organiser a phwandoli atitsimikizilq kuti patsikuli kukakhala oimba osiyana siyana kuphatikizaposo oimba odziwika bwino muno mmalawi monga Mad Dotolo wamabilinganya empire ndi ena ambili.

Patsikuli Djee Phaxy Mw wakonzeka kukaipatsa moto ndipo Kizito Precious Matiki ndiye akayendetse mwambowu patsikuli.

Iwo ati akupelekaso mwayi kwa oimba ena amene akufuna kuzaonesa lush lawo kwa anthu amene ataxabwele patsikuli kui alembetse kudzela ku 0882430605.

šŸ—£šŸ—£ Hello eee ndikuti ndatsika ndaimq pafupi ndi njinga ...undiona ndatchena ndipo ndamatchisa zovala za ku ntchito🤣🤣🤣Tam...
24/10/2024

šŸ—£šŸ—£ Hello eee ndikuti ndatsika ndaimq pafupi ndi njinga ...undiona ndatchena ndipo ndamatchisa zovala za ku ntchito🤣🤣🤣
Tamutchuleni mnzanu amene angavale chonchi adziwe kuti mumamunyadila..

Komatu anthu simuyankhula bwino...Dr Namadingo simunthu osewela naye
23/10/2024

Komatu anthu simuyankhula bwino...Dr Namadingo simunthu osewela naye

Let's vote for Tabitha TC11 Chawinga via this linkHere are my   2024 winners, vote for your winners
08/10/2024

Let's vote for Tabitha TC11 Chawinga via this link
Here are my 2024 winners, vote for your winners

Here are my 2024 winners, vote for your winners

Tiyeni ku Banja la mtsogolo
06/10/2024

Tiyeni ku Banja la mtsogolo

Komatu zimene akupanga  Mabedi eeeeeee Kwinako titukwanašŸ˜’šŸ™„  @followersMabedimustfall
04/10/2024

Komatu zimene akupanga Mabedi eeeeeee Kwinako titukwanašŸ˜’šŸ™„


@followersMabedimustfall

Biography !Sangie is a young girl who does reggae. She started music while very young and is a qualified vocal trainer. ...
02/10/2024

Biography !

Sangie is a young girl who does reggae. She started music while very young and is a qualified vocal trainer.

She however, did not take music seriously and hence her main acts in music had been backing up other artists and church choir. Born Angel Mbekeani, Sangie has grown up in Blantyre (Ndirande) and made her first single, ā€œI do it all for loveā€ only this year (2014) when she attempted the Don Foxxy Riddim.

The Riddim was initially produced in 2012 by Don Foxxy at Step Up Records and had featured other artists such as Nepman, Desert Eagle, Vigil, Saint and Nepman. ā€œI do it all for loveā€ which was released as a video, topped Makwerero 10 on MBC TV for a month and has enjoyed airplay on various TV stations.

Sangie, is a Malawian reggae artist and songwriter.In 2015, she won as the best female artist of the year in UMP Awards.In 2016 and 2019, she was nominated in the same awards in Best Female Artist of the Year.In 2017, she won in the same awards in Best Female Act.

Follow the page for more updates
Our WCW Sangie

Anthu a ku Zomba , Bamboo ake a Lino wa apaseni plot.....Chiyambileni kuimba Robert WinterCharge Mwanyali anatengelatu m...
30/09/2024

Anthu a ku Zomba , Bamboo ake a Lino wa apaseni plot.....
Chiyambileni kuimba Robert WinterCharge Mwanyali anatengelatu malo a ma guys ena a mu Archaida

Lero WinterCharge akhala kutulutsa track ina pa made On Monday....uyu sakhumudwisa uyu

Anthu awa anabadwa lero...Monica ChakweraAnjiru FumulaniPano pabwalo tingoti zabwino zonse kudzaka za tsopano
30/09/2024

Anthu awa anabadwa lero...
Monica Chakwera
Anjiru Fumulani
Pano pabwalo tingoti zabwino zonse kudzaka za tsopano

Malinga Mafia & Sangie kuswitilana ...Akhalitse mbuye shiva🫔
29/09/2024

Malinga Mafia & Sangie kuswitilana ...Akhalitse mbuye shiva🫔

Address

Area 49, Street 2
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pabwalo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share