
02/02/2025
MBIRI YA NYASA BIG BULLETS.....................................
*Big bullets inayamba mu chaka cha
1967 .
*Imatchedwa team ya fuko , maule
kapena mapale ndi anthu
Oyitsatira.
*Bullets yapambana chikho cha
Super league of Malawi ma ulendo
okwanira 16 , kuposa team ina
iliyonse m'Malawi.
*Imagwilitsa ntchito Kamuzu
Stadium, ngati pakhomo pawo ,
Koma pakadali pano
Nyumba sadadzimangire.
*Mpikisano waukulu uli pakati pa
Big bullets komanso Mighty
Wanderers pa ufumu wa mpira
Mu mzinda wa Blantyre.
*Bullets yapikisanako ndi ma team
Ena akuluakulu muno mu Africa,
Mu mipikisano ya African Cup
Champions ndi Caf Champions
League.
*Yapambanako Dzikho monga Super league of Malawi, Malawi Carlsberg Cup ,Fam Charlity shield.
Follow Did you know ? Kuti mudzinva nkhani zosiyanasiyana.