Better TV Malawi

Better TV Malawi WE ARE HERE TO SHARE ISSUES WITH FRIENDS AND RELATIVES

28/07/2026
28/07/2026

Phungu wa Mzuzu City North Frasco Mkandawire wapepha boma kuti liwamangire police unit pa Luwinga pomwe pali police unit yomwe yili mu nyumba ya a Singini

Ndipo a Mkandawire ati anduna woona za chitetezo a Peter Mukhito ati ndiwozipereka kudzera ku council kuti police unit yimangidwe mdera la Luwinga

Zambiri akufotokoza motere mu kanema iyi

28/07/2026

Phungu wa Ntchisi North Constituency Arnold Kadzanja wapepha boma kuti liwamangire mpanda pa school ya Masongole CDSS ndi cholinga choti ana aziphuzira bwino opanda kumva phokoso la mseu wa tala.

Iwo ati sanankhutire ndi yankho lomwe anduna azama mphunziro Bright Msaka awayankha ndipo pali chiyembekezo choti awafikiraso anduna azama mphunziro.

A Kadzanja akufotokoza zambiri mkanema iyi

27/07/2026

Phungu wa Dedza Boma Constituency Howard Mzambweuluemba wapepha boma kuti liwamangire mpanda pa school ya secondary ya Umbwi komaso kuti awamangire CDSS yina mdera lawo

Mzambweuluemba ati anduna awayankha bwino ndipo ali ndichinkhulupiriro kuti awamangira zitukuko ziwiri zomwe apempha lero mu nyumba ya malamulo

Iwo akufotokoza zambiri mkanema iyi

27/07/2026

Zingayambe kuyiwalika
FULL TIME

Mighty Wanderers FC 1-1 Masters FC

Neba ukuva bwanji kumeneko?

26/07/2026

Ma player a Dedza alowa mu Stadium atabelekedwa kuopa kuchesulidwa

Dedza Dynamos 1 Bullets 0 at Dedza Stadium

24/07/2026

Phungu wa Chitipa North Constituency Faless Debrah Mpoha Moyo wapepha boma kuti liwamangire ma police units ndi cholinga choti mdera lawo mkhale chitetezo chokwanira

Mpoha Moyo ati mdera lawo linapanga malire ndi Zambia komaso Tanzania nde kukufunika chitetezo chachikulu ndi cholinga choti anthu a mdera limeneli ankhale otetezedwa

Mpoha Moyo akufotokoza zambiri mkanema iyi

24/07/2026

Phungu wa Chiradzulu Nyungwe Constituency Mwayi Ndalama wati ndiwokhutira ndi yankho lomwe anduna azama mphunziro Bright Msaka ayankha dzulo mu nyumba ya malamulo

A Ndalama amafuna secondary school ya mdera lawo yinkhala ndi nambala yoti ana a school azilembera mayeso a maneb pa school pomwepo

A Ndalama ati unduna wa zamaphunziro ulankhulana ndi a maneb kuti ma school wa ankhale ndi ma nambala olembera mayeso a maneb

A Ndalama akufotokoza zambiri mkanema iyi

23/07/2026

Mizati Band Live at BICC

22/07/2026

Phungu wa Blantyre South East Constituency Jeremiah Jumbe wapempha boma kuti liwathandiza vuto lakusowa kwa madzi mdera lawo.

Iwo polankhula lero mu nyumba ya malamulo ati anthu aku Chilobwe akusowa madzi ndipo pakufunika boma lichitite machawi powapatsa madzi kudzera ku Blantyre Water Board.

A Jumbe ati ndiwonkhutira ndi yankho lomwe boma lapereka lero ndipo ali ndi chinkhupiliro kuti boma liwapatsa madzi awu nkhondo.

A Jumbe akufotokoza zambiri mkanema iyi

Address

Lilongwe

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00
Sunday 09:00 - 17:00

Telephone

884280200

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Better TV Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Better TV Malawi:

Shortcuts

Share