Online bible study.

Online bible study. Mau a mulungu ndia ulele phuzilan kut moyo wanu wauzimu ukhale owala. Zomwe mulinazo phuzisan azanu kut aziwe.

Ngat muli ndi fuso lili lose lokhuza baibulo chonde tumizani uthenga SMS ku tigawane bib.

08/07/2025

Chisomo cha ambuye chikufikilen

07/07/2025

Pak*ti timadziwa siku lakubadwa,koma lakufa sitiziwa Ambuye tetezani miyoyo yathu usiku oopsau kt mawa tilioneso

07/07/2025
07/07/2025

Congratulations 🎉🎉🌹🌹

07/07/2025

Mulungu amatikonda chifukwa tili ndi moyo

07/07/2025

Mulungu ndiwabwini 🙏🙏

06/07/2025

Mulungu atiteteze usiku opsau

06/07/2025

MATEYU 6 : 24

Palibe munthu angathe kukhala kapolo wa ambuye awiri: pak*ti pena adzamuda mmodziyo, ndi kukonda winayo; pena adzakangamira kwa mmodzi, nadzanyoza wina. Simungathe kukhala kapolo wa Mulungu ndi wa Chuma.

05/07/2025

Auzen k*t za mulungu sitipangila mpikisano
GOOD morning

04/07/2025

Kupulumuka ndichisomo cha Mulungu

Address

Kanengo
Lilongwe
KANENGO

Telephone

+265991893937

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Online bible study. posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share