Wings Of The DOVE

Wings Of The DOVE Creating knowledge in your mind β™§ Those who were friends at school must continue being our friends & also who were haters must also continue being enemies.
(6)

Do not try be friendly just because you've meet at a certain place which all of are intrude no no no that's very bad. THIS IS JOZY'S FIRST LAW OF FRIENDSHIP. -KAYZ Β©[email protected]

With these photos I think ambiri tikuenera kuphunzirapo chinachake.This is so painful, not only for the guys who are in ...
25/06/2026

With these photos I think ambiri tikuenera kuphunzirapo chinachake.
This is so painful, not only for the guys who are in those photos, but for all of us as a country.

Zithunzi izizi zizikhala zikuwaliza amene ali mu ma photos and ma family awo azizivera chisoni.
Ndizovesa chisoni kuti mmene zakhaliramu after 2 to 3 months ena akhala atayambaso kufuna kubwerera komweko.πŸ’”
Guys let's try to work hard tili kwathu komkuno, coz kunotu life is simple than ku South Africa, we move freely even if people knows kuti wanyamula ndalama Zambiri.

Look, some of these guys have spent more than 10yrs in South Africa, see how are they coming? Ena anali komkuno koma anapusha within the same yrs panopa zawo zili pabwino.

Panopa kuchoka malawi to South Africa kuenda pa bus munthu amaononga close to MK800,000. With such amount you can start ka business kako komkuno ndikumasuntha. Koma moyo okhalira chewu chewu Uwuwu ndiochitisa mantha kwambiri πŸ˜₯😭

Tukwanani ndi ufulu wanu bola ndanena maganizo anga 😣

Kaya zikuveka kumbuyoko πŸ™„Osakakamiza zinthu mutenga nazo mabomu aweni πŸ˜‚
23/06/2026

Kaya zikuveka kumbuyoko πŸ™„
Osakakamiza zinthu mutenga nazo mabomu aweni πŸ˜‚

Breaking news.Mmodzi mwa ma membala a SMAM wadandaula ndi mchitidwe wa anthu omwe amapakira soya pieces wa Top Soy.Memba...
22/06/2026

Breaking news.
Mmodzi mwa ma membala a SMAM wadandaula ndi mchitidwe wa anthu omwe amapakira soya pieces wa Top Soy.

Membalayu wadandaula atapeza soya pieces okwana 23 mu packet kwinako atapakira mpweya 😣
Mchitidwewu ukupitirira kukulira kulira mdziko muno 😌

Pali iPhone x Pro casket iyi amene angaifune tivane kamtengo wez πŸ‘Œ
22/06/2026

Pali iPhone x Pro casket iyi amene angaifune tivane kamtengo wez πŸ‘Œ

You don't need anyone to decide who you must be. Design, create and allocate yourself, who, where and how you should be ...
21/06/2026

You don't need anyone to decide who you must be. Design, create and allocate yourself, who, where and how you should be πŸ‘Œ
When life always gives you lemons, you can turn it into lemonade and enjoy it πŸ€—
Always create yourself a room where good luck will find you 🀩

Basi ndikapanga page ilionse ikangoyamba kuthamangisa ma followers mumalimbana nane πŸ™„Ndazisiya sinadyeko ndalama za mone...
20/06/2026

Basi ndikapanga page ilionse ikangoyamba kuthamangisa ma followers mumalimbana nane πŸ™„
Ndazisiya sinadyeko ndalama za monetization ine.
Ndipitiliza njira zomwe masikira ndalama, izizi ndazisiya.
Mukandiona pano zingobwerera macheza Osati za serious πŸ‘Œ
πŸ™

20/06/2026

Komatu nde sizikubeba πŸ€¦β€β™‚οΈ

I accepted 5 fan badges from Thokozani Ntenda, Maureen Nangozo Kachingwe and 3 others.
18/06/2026

I accepted 5 fan badges from Thokozani Ntenda, Maureen Nangozo Kachingwe and 3 others.

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Wings Of The DOVE posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Wings Of The DOVE:

Share