Chinkhwiri Media

Chinkhwiri  Media CHINKHWIRI MEDIA
Pezani nkhani zosiyana siyana

OSAIWALA KUPANGA



23/05/2026

BLUE EAGLES 1 vs BULLETS 1

Kodi ku BULLETS zikuvuta pati kapena coach asanakhazikike???
osaiwala kupanga follow Chinkhwiri Media

23/05/2026

Zosayenda ku Banja la MAULE
Kodi Vuto ndi COACH kpn MA PLAYER??
Inu mukuona kuti Vuto nichan Pelekani maganizo anu m'mene mukuonela.
Thanks 🙏 timakunyadilan Maule
Osaiwala kupanga follow Chinkhwiri Media

23/05/2026

Zosayenda ku Banja la MAULE
0 kwa 0
Kodi Vuto nichan tive maganizo anu Maule??
osaiwala kupanga follow Chinkhwiri Media

ZOTHANDIZA MZIMU  Part 1(I) DZIWANI MPAMVU ILI MKATI MWANU.Dziwani mphamvu yomwe ili mkati mwanu, ndipo simudzavutikanso...
21/05/2026

ZOTHANDIZA MZIMU Part 1

(I) DZIWANI MPAMVU ILI MKATI MWANU.
Dziwani mphamvu yomwe ili mkati mwanu, ndipo simudzavutikanso ndi mzimu wokhumudwa.
Ndipo kodi mphamvu yamkati imeneyi ndi chiyani? Kungoti mphamvu yochokera kwa Mulungu siingakhulupirire. Kufikira pamlingo womwe mukukula luso ili, mudzapambana kugonjetsedwa m'moyo wanu. Nkhani yaikulu ndi kuphunzira kukhulupirira. Izi zayamba mu imodzi mwa ndime zofunika kwambiri m'Malemba.

Yesu anati kwa iye, "Ngati mungathe kukhulupirira, zinthu zonse n'zotheka kwa iye amene akhulupirira." ( Marko 9:23 )

Phunzirani kukhulupirira. Phunzirani kuchotsa kukayikira.
Izi zimachitika mwa kuchita kutsimikizira. Tsimikizirani chikhulupiriro.
MULUNGU AKUDALITSEN NONSE:

Osaiwala kupanga follow Chinkhwiri Media Kuti zisamakhuphonyeni

20/05/2026

Osaiwala kupanga follow page

Inu mutsata ziti  Tsatani yesu ndiyo njila ya zonse Osaiwala kupanga follow Chinkhwiri  Media
20/05/2026

Inu mutsata ziti Tsatani yesu ndiyo njila ya zonse
Osaiwala kupanga follow Chinkhwiri Media

20/05/2026

Mayi Jessy kabwila kuyankhatu kumeneko k*k

20/05/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Christopher Meza, Kondwan Goba

17/05/2026

osaiwala kupanga follow page

17/05/2026

Follow page

Maule kod Mwakozeka???Osaiwala kupanga follow Chinkhwiri  Media
17/05/2026

Maule kod Mwakozeka???
Osaiwala kupanga follow Chinkhwiri Media

Address

Chinkhwiri
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chinkhwiri Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share