Okonda UTM

Okonda UTM Economic Revolution.

02/11/2025

DK anali pa Mwanza lero very nice 😎

02/11/2025

Olo magetsi atazima kwa chaka chonse ife nde Chakwera sitingamufunebe. Ya SKC imatiwawabe mpaka pano 😎

Lero ku Mwanza 😎
02/11/2025

Lero ku Mwanza 😎

31/10/2025

Anyamata azikwanje anatulutsidwa pa belo aja anjatidwaso. Nyimbo ikhale iti anzanga a UTM amene tikumva kukoma ku opposition 😎

Akaluza MCP, olakwa ndi ovota. Akaluza wa UTM, kachipani kanatha. Eh koma ku opposition nkobhebha 😎
31/10/2025

Akaluza MCP, olakwa ndi ovota. Akaluza wa UTM, kachipani kanatha. Eh koma ku opposition nkobhebha 😎

Ngakhale China imaziwa kuti kuli Dr Dalitso Kabambe. Basitu kumuitana DK pa 76 anniversary ya Republic of China. 😎
31/10/2025

Ngakhale China imaziwa kuti kuli Dr Dalitso Kabambe. Basitu kumuitana DK pa 76 anniversary ya Republic of China. 😎

30/10/2025

Anyamata azikwanje ija: akuti kupatula mlandu womenya Namiwa, ali ndi milandu ina 10. Kumalemekeza apolice amafinya anyamatawa 😎

30/10/2025

Muzonse yamikani Mulungu. Ife phee kumva kukoma pa 4% 😎

30/10/2025

Kenako Chimwendo Banda azikati Mr Speaker Sir! Kunena Sulemani. Eh dziko ili... 😄😄 😎

29/10/2025

Anyamata azikwanje akana mulandu. Zikatele akazaluza mulandu amakhala kuti aziwonjezera chilango chifukwa chochedwetsa a khothi 😎

29/10/2025

Dr Catherine Mzumara we wish all the best 😎

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Okonda UTM posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share