15/05/2025
KU INTERVIEW
interviewer: takulandiran Mr G,
mwakonzeka kuyankha zomwe
tikufunseni?
G: ndili okonzeka sir
Interviewer: inuyo mukuyendetsa
galimoto
yanu ndipo mukudutsa malo ena
mwapeza
anthu atatu omwe akudikira transport.
wina ndi
mzanu yemwe anak*thandizan
mutachita ngozi
mutasala pang'ono kumwalira, wina
ndi munthu
wammayi wachikulire ndithu wadwalika
kwambiri akupita kuchipatala komanso
pali
mkazi yemwe mwakhala
mukumuganizira
ndikumulota mumafuna atakhala wanu,
Pa
anthu atatuwa galimoto yanu ikuyenera
k*tenga
mmodzi chifukwa ndiyoyenera anthu
awiri, kodi
mungatengepo ndan? Mukatenga
yemwe
anak*thandizani pangoziyu ikhala ngati
mbalidwe
yomuthokoza, kusiya mkaziyo ndek*ti
simuzakumana nayenso mmoyo wanu,
kusiya
mmayi odwalayu ndek*ti zamoyo wake
simusamala. Mungatenge ndan?
G: ndimmene zililimu ndikhoza
kungopereka makiyi agalimoto kwa
nzanga
anandithandiza pangoziyo k*ti
amutengere
odwalayo kuchipatala ine nditsala ndi
mkaziyo
pomwepo.
Interviewer: congrats sir u've made
it
ONE WORD TO G PLEASE
---