Mkulima Bola Farms

Mkulima Bola Farms Use your time to make money until your money buys back your time.

(5)

09/04/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Chilambula D. Mary, Hayidar Rayaa, Shally Allan Danger, Øg Innoce Innoce, Precious Kadondo

06/04/2026

Big shout out to my newest top fans! Bwana Miyuzi, Andy Andrews Andrew, Esmy Kambalame, Pemphero Chiusiwa

Kuweta nkhuku za madzira (layers) kumafuna kukonzekera bwino ndi kasamalidwe kolondola. Lero Tiyeni tifotokozerane  mosa...
22/03/2026

Kuweta nkhuku za madzira (layers) kumafuna kukonzekera bwino ndi kasamalidwe kolondola. Lero Tiyeni tifotokozerane mosavuta momwe tingachitire:

1. KONZANI KHOLA LANU LABWIINO
Khola likhale loyera, louma, komanso lotetezeka ku mphepo ndi mvula

Musazipanikize (osakhala mothithikana)

2. SANKHANI MTUNDU WABWINO WA NKHUKU ZA MADZIRA
Gulani ma chicks kuchokera kwa ogulitsa odalirika

Sankhani nkhuku za madzira (layers) osati za nyama

3. PEREKANI CHAKUDYA CHOYENERA
Gwiritsani ntchito chakudya cha ma layers (layer feed)

Onetsetsani k*ti nthawi zonse ali ndi madzi oyera

Chakudya chikhale chokwanira k*ti ziziyikira bwino

4. SAMALANI THANZI LA NKHUKU ZANU
Perekani katemela nthawi yake

Sungani ukhondo wa khola nthawi zonse

Yang’anirani matenda msanga

5. KUWALA (light management)
Nkhuku za madzira zimafuna kuwala kokwanira (maola 14–16 patsiku) k*ti ziziikira bwino

Usiku mungagwiritse ntchito nyali

6. SUNGANI MADZIRA PABWINO NDINSO POTETEZEKA
Sonkhanitsani mazira tsiku ndi tsiku

Sungani pamalo oyera komanso ozizira

7. KHALANI NDI MISIKA YODALILIKA
Pezani makasitomala (ma shop, ma hotel, anthu payekha)

Khalani odalirika pa supply ya mazira

Chofunika kwambiri:
Kupirira, kusamalira bwino, ndi kuyang’anira tsiku ndi tsiku ndi zomwe zimapangitsa k*ti ulimi wa ma layers ukhale wopambana.

Shamrisah farm investments - pecking at perfection, delivering quality
wise poultry farms





19/03/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Pearson Pèèbouy Mwale, Monalisa F Mbukwa, Esmy Kambalame, Zeb Malenga, Bright Gonani, David Nkhata, Rajab Chikuni, Lanziel Milanzi, Rainey Davis Manyamba, Lovemore Mgona, Titus Aloke, Professors Costa P Chilomo, Mage Chunga, Adjar Kajal, Charles Bugumba

Urgent sale of chickens ma kroilers . almost point of lay. K 15000 each . give away price!0889500722Kasungu
16/03/2026

Urgent sale of chickens ma kroilers . almost point of lay. K 15000 each . give away price!
0889500722
Kasungu

16/03/2026

Big shout out to my newest top fans! Andrew Prince Hiwa, Esmy Kambalame

14/03/2026

Ma hyliens chicks nde ayamba k*tumizidwa mawa

14/03/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Betso Betsolistics Ngundu, Dalitso Chikafumbwa, Alinafe Kankhande, Peter B Nyirenda, Jeremiah Nephan, Jenifer Kamwendo, Precious Twalibingi Kisyombe, Harry MW, Joseph Mandala, Anthony Nyang'wa, Evelin Kabano, Tadala Muthali, Pemphero Chiusiwa, Dorothy Chintokoma Phiri, Pemphero Chiusiwa, Deborah Kapingasa, Thandie Sanga, Ulem Jonathan, ɭɭ Achipala ɭɭ, Grevazio Paweck, Grazd Sruth, Joseph Ignacio Nehiya, Dickson Bright Mwale, Stayeen Anafi, Manzyman Zonge Chikankhen, Thothi B Jáh Śeeđ, Rachel Chunga, Keepson Charles Ntaya, Selina Phiri, Jameela Size, Alinafe Banda Kaliati, Inno Mosse, ɭɭ Bornfrée ɭɭ, Said Ali, Wittie Beib Wa Walata, Barton Njolwa, Jane Mgomezulu, GD JOMENI KHULANI, William Kantunda, Bwana Miyuzi, Mercy Mbambo, Lickson Zulu, Påçhæłœ Ñķ, Collins Nasiyaya, Kapalamula Chax, Leo Philles, Máy Day, Mickson Mwale, LiQue Ngah

14/03/2026

katundu ndi ameneyu mawa tikuyamba k*tumiza. tilankhuren k*t nanuso mugureko Anu ma hyline chicks

12/03/2026

local chickens and Hy lines for sale month and 5days old at affordable prices kuyambira nkhuku ten kupita mwamba

Malawi AgriBiz Podcast   muzawauendereko akulu awa ndi good example kumalawi kuno Yanjanani Khongoni kenako ife Mkulima ...
12/03/2026

Malawi AgriBiz Podcast muzawauendereko akulu awa ndi good example kumalawi kuno Yanjanani Khongoni kenako ife Mkulima Bola Farms

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mkulima Bola Farms posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share