Prophet Peter Phiri

Prophet Peter Phiri Mulungu wositha Nyengo asitheso zanu ndipo kudziwike Kuti Mulungu Ali Nanu Amen 🙏

Pemphero ndi key Mulungu akatsegula khomo palibe wina matseka palibe wopondeleza Mulungu ayakhe mapemphero ako mudzina l...
12/08/2026

Pemphero ndi key

Mulungu akatsegula khomo palibe wina matseka palibe wopondeleza

Mulungu ayakhe mapemphero ako mudzina la Yesu khristu

tikumane ku botanic garden muzinda wa Lilongwe nthawi 8:00 mamawa

Tsiku pa 14 August 2026 Friday

Ndikutsutsana nalo lilime lokulankhulira matsoka pamoyo wako Ndikuphwanya ndikupasula mabwalo wokutembeleraAmene Ali ndi...
05/08/2026

Ndikutsutsana nalo lilime lokulankhulira matsoka pamoyo wako

Ndikuphwanya ndikupasula mabwalo wokutembelera

Amene Ali ndimau otsiliza a payiwe ndi Ambuye Yesu khristu

Mulungu akuze malile ako in Jesus Christ name

Pangani follow page ya Prophet Peter Phiri kuti zambiri zisakuphonyeni lero

Nyengo zingalimbe bwanji koma nthawi imafika yoti Mulungu amakukumbukila Lero Mulungu akupatse umboni pamoyo wako mudzin...
30/07/2026

Nyengo zingalimbe bwanji koma nthawi imafika yoti Mulungu amakukumbukila

Lero Mulungu akupatse umboni pamoyo wako mudzina la Yesu khristu

Dzuwa Lisanalowe China Chake Chatsopano chichitike pamoyo wako in Jesus Christ name

Mulungu abwezeletse zomwe Satana anakubela pamoyo wako mudzina la Yesu khristu. Join me Sunday service

Kuyambila lelo moyo wako udzidutsa muzokoma osati muzokhoma kuyambira lero in Jesus Christ name Pangani follow page ya P...
19/07/2026

Kuyambila lelo moyo wako udzidutsa muzokoma osati muzokhoma kuyambira lero in Jesus Christ name

Pangani follow page ya Prophet Peter Phiri kuti zambiri zisakuphonyeni lero

Mulungu sanakulenge kuti udzangokhala moyo Ovutika moyo wako Onse Nthawi yoboleza imakwana ndipo ya kwana .Join man of G...
18/07/2026

Mulungu sanakulenge kuti udzangokhala moyo Ovutika moyo wako Onse

Nthawi yoboleza imakwana ndipo ya kwana .

Join man of God Lero 7:30 madzulo pamene akhale akupemphelera Onse omwe akufuna kubowoleza.

Palibe chomwe Mulungu chingamulake ndipo Lero asintha nyengo ZAKO mudzina la Yesu khristu

Pangani follow page ya Prophet Peter Phiri kuti zambiri zisakuphonyeni lero

Guwa lopondereza mwayi wako ndi madalitso ako, lisweke lero in Jesus Christ name Lero Mulungu akukumbukile akupatse umbo...
17/07/2026

Guwa lopondereza mwayi wako ndi madalitso ako, lisweke lero in Jesus Christ name

Lero Mulungu akukumbukile akupatse umboni wakulu iweyo amene ukuwelengawe

Zichitike ndi moyo wako mudzina la Yesu khristu

Pangani follow page ya Prophet Peter Phiri kuti zambiri zisakuphonyeni lero

MULUNGU wanu sakuchititsani manyazi Zitheka zomwe mwapempha mudzina la Yesu  KhristuAroma 10:11 "Pakuti Malemba anena, A...
13/07/2026

MULUNGU wanu sakuchititsani manyazi

Zitheka zomwe mwapempha mudzina la Yesu Khristu
Aroma 10:11 "Pakuti Malemba anena, Aliyense wokhulupirira Iye sadzachita manyazi

Lero Mulungu azionetsela yakha pamoyo wako in Jesus Christ name

Lero Monday Mulungu akukumbukile in Jesus might name Lero Mulungu akukumbukile wakhalitsa panthamanda lamavuto matenda k...
13/07/2026

Lero Monday Mulungu akukumbukile in Jesus might name

Lero Mulungu akukumbukile wakhalitsa panthamanda lamavuto matenda kusowa ntchito kusowa banja kusowa ndalama

Lero Mulungu apange zayiwe mudzina la Yesu khristu

Pangani follow page ya Prophet Peter Phiri kuti zambiri zisakuphonyeni lero

Khomo lako likatsekeka Mulungu amatsegula linaLero Mulungu azionetsele yekha pamoyo wako in Jesus Christ name
11/07/2026

Khomo lako likatsekeka Mulungu amatsegula lina

Lero Mulungu azionetsele yekha pamoyo wako in Jesus Christ name

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Prophet Peter Phiri posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share