Mtunda Sport

Mtunda Sport Sports News And Updates

Mukuganiza Kuti LERO babatunde achinya zigoli zingati ?
25/09/2026

Mukuganiza Kuti LERO babatunde achinya zigoli zingati ?

Adiel Kaduy🔥Tikuti South Sudan ikhawula
25/09/2026

Adiel Kaduy🔥

Tikuti South Sudan ikhawula

Pangolin nominated for Ballon Dior...Ichichi nthawi yovota ikayamba tivota mpaka chinthuchi titenge.
09/09/2026

Pangolin nominated for Ballon Dior...

Ichichi nthawi yovota ikayamba tivota mpaka chinthuchi titenge.


Silver Strikers yasankha technical  panel yongogwilizira yomwe itsogoleledwe ndi a Patricio Kulemeka amene amaphunzitsa ...
09/09/2026

Silver Strikers yasankha technical panel yongogwilizira yomwe itsogoleledwe ndi a Patricio Kulemeka amene amaphunzitsa timu ya Silver Strikers ya atsikana.

Kulemeka atsogolera panel second round ya FDH BANK PREMIERSHIP ikamayamba.

Mabanka ndizomwe mumayembekezera?, anyway poti ndiongogwirizira.


Enos Chatama yawuma ku Ekhaya.Inu ntchito zama coach zikungotha anga chibwezi🤣
08/09/2026

Enos Chatama yawuma ku Ekhaya.

Inu ntchito zama coach zikungotha anga chibwezi🤣


Peter Mgangira yauma kuma Banker.Nanga 5 zero uja chidachitika chija chipongwe inu.
08/09/2026

Peter Mgangira yauma kuma Banker.

Nanga 5 zero uja chidachitika chija chipongwe inu.


Chi Sulumba Chija achiyambitsa.umu ndimene Nginde Macdonald wayiyambitsila team Wanderers masana ano pamene ikhale ikukw...
06/09/2026

Chi Sulumba Chija achiyambitsa.

umu ndimene Nginde Macdonald wayiyambitsila team Wanderers masana ano pamene ikhale ikukwapula team ya Simba Mumpikisano wa CAF

⏰ 3pm

06/09/2026

Mwakwera itiyo

Everton kapena Man United?

Team News is here

🏴󠁧󠁢󠁥󠁮󠁧󠁿 Everton XI: Pickford; Röhl, Tarkowski, Branthwaite, Mykolenko; Garner, Armstrong; Dewsbury-Hall, Johnson, George; Barry

🏴󠁧󠁢󠁥󠁮󠁧󠁿 Man Utd XI: Lammens; Dalot, Maguire, Martínez, Shaw; Tielemans, Mainoo; Mbeumo, Fernandes, Rashford; Cunha

This is how Ekhaya has lineup against KARONGA UNITED the ingwina
06/09/2026

This is how Ekhaya has lineup against KARONGA UNITED the ingwina

06/09/2026

KARONGA UNITED STARTING XI AGAINST EKHAYA FC

GOALKEEPER
1. Richard Nyirenda

DEFENDERS
22. Pilirani Thulu (C)
3. Innocent Chitete
2. Nangie Songa
44. Thomas Khunga

MIDFIELDERS
5. Yusuf Adesola
8. Chimwemwe Myombe
66. Antony Mwalilino

ATTACKERS
21. Michael Mwalilino
20. Tambulani Mwale
24. Samson Sokanya

SUBS
50. Gracian Kazembe
6. William Mwalwimba
53. Lumbani Kamtoma
23. Wakisa Mwasamata
16. Alick Austin
26. M***a Kishombe
25. Raphael Nkhoma
30. Kennedy Mwakabaghe

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mtunda Sport posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mtunda Sport:

Shortcuts

Share