Nyombe Media

Nyombe Media Nyombe Media 🇲🇼
News • Laughs • Street Vibes • Everything Malawi
Daily posts | Live every Sunday 8PM
DM for Promos & Collabs 📩
(1)

Nde Chatchuka. Congratulations a Chimwemwe wa Chimwemwe 🥳
27/08/2026

Nde Chatchuka. Congratulations a Chimwemwe wa Chimwemwe 🥳

Nigerian star. *Tiwa Savage*🥲
26/08/2026

Nigerian star. *Tiwa Savage*🥲

Koma uyo ndotopetsa Eeh🙌🏻 ati kuongola minyewa😅
20/08/2026

Koma uyo ndotopetsa Eeh🙌🏻 ati kuongola minyewa😅

Basi ana aja achikwapula. President Professor Arthur Peter Mutharika has awarded each Scorchers player K5 million. First...
20/08/2026

Basi ana aja achikwapula. President Professor Arthur Peter Mutharika has awarded each Scorchers player K5 million. First Lady Professor Gertrude Mutharika made the announcement during a luncheon she hosted in honour of the team.

Katswiri wa nyimbo Kell Kay wapereka nyimbo yake yatsopano ‘Wale’ ngati mphatso ya ulemu kwa timu ya Schotchers. Iye wat...
20/08/2026

Katswiri wa nyimbo Kell Kay wapereka nyimbo yake yatsopano ‘Wale’ ngati mphatso ya ulemu kwa timu ya Schotchers. Iye wati asungwana ododa chikopawa abweletsa ulemu wa ukulu ku dziko lino ndipo asadandaule kuti sanatenge chikho.

Polemba pa tsamba lake la Facebook, anati Scorchers ipeze chilimbikitso ku nyimbo yi yomwe imalimbikitsa anthu kuti azivomereza zotsatira zomwe ziwachitikira mmoyo, kulekana ndi kulira pa zinthu zomwe sanakwanilitse.

Lunch Hour. Kalibu 😊
20/08/2026

Lunch Hour. Kalibu 😊

Simmene kuliri. Eeh🙌🏻
19/08/2026

Simmene kuliri. Eeh🙌🏻

Ndim'mene zinalili masanawa ku bwalo landende ku Lilongwe
19/08/2026

Ndim'mene zinalili masanawa ku bwalo landende ku Lilongwe

Koma Bwezi mwatipatsa nyimbo, ah ah ku Madness akuti chani Kodi.?
19/08/2026

Koma Bwezi mwatipatsa nyimbo, ah ah ku Madness akuti chani Kodi.?

Address

Area 24
Lilongwe
132-567

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nyombe Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share