OpenEye Magazine

OpenEye Magazine πŸ“° News | 🎭 Culture | πŸ—£οΈ Youth Voices
πŸ‡²πŸ‡Ό Opening eyes to Malawi’s real stories & perspectives

🚨 BREAKING NEWSπŸ‡²πŸ‡Ό Brian Banda, MBC Director General, has died following a short illness.πŸ•ŠοΈ May his soul rest in peace.OP...
08/08/2026

🚨 BREAKING NEWS

πŸ‡²πŸ‡Ό Brian Banda, MBC Director General, has died following a short illness.

πŸ•ŠοΈ May his soul rest in peace.

OPENEYE MAGAZINE2026

Monga amanenera mafani, "Yamal akayamba, Spain siphonya." πŸ”₯πŸ‡ͺπŸ‡Έ
14/07/2026

Monga amanenera mafani, "Yamal akayamba, Spain siphonya." πŸ”₯πŸ‡ͺπŸ‡Έ

Bro code siyongolankhula basi. Ndi kukhulupirika, ulemu, ndi kuthandizana nthawi zonse. Real bros stay real. πŸ’ͺπŸ”₯         ...
13/06/2026

Bro code siyongolankhula basi.

Ndi kukhulupirika, ulemu, ndi kuthandizana nthawi zonse. Real bros stay real. πŸ’ͺπŸ”₯


πŸ”₯ BIG NEWS! πŸ”₯Malawi's music industry keeps growing! 🎢Mfana wa mu Bangwe Zonke Too Fresh has officially joined Madness En...
06/06/2026

πŸ”₯ BIG NEWS! πŸ”₯

Malawi's music industry keeps growing! 🎢
Mfana wa mu Bangwe Zonke Too Fresh has officially joined Madness Entertainment and will now be known as Zonke Madness. πŸš€

With this new addition, Madness Entertainment yakwanitsa 6 male artists, making the camp even stronger and more competitive.

The question is: Who should be the next artist to join the Madness family? πŸ‘€πŸ”₯

06/06/2026

Achina Thomas πŸ˜‚πŸ˜†

πŸ˜”πŸ’” Sad newsMalonie Kyz wafotokoza kuti usiku watha akuba analowa m'nyumba mwake ndikuba foni yake, foni ya brother wake,...
06/06/2026

πŸ˜”πŸ’” Sad news

Malonie Kyz wafotokoza kuti usiku watha akuba analowa m'nyumba mwake ndikuba foni yake, foni ya brother wake, ma bedsheet, komanso hustle bag yomwe amayika ndalama.

Tikukhulupirira kuti zinthu zake zibwezedwa ndipo omwe achita izi apezeke.

πŸ“° OpenEye Magazine

πŸ€”β€οΈ N'chifukwa chiyani anthu akakhala pa chibwenzi kwa nthawi yayitali amayamba kufanana?Ena amati ndi chifukwa choti am...
06/06/2026

πŸ€”β€οΈ N'chifukwa chiyani anthu akakhala pa chibwenzi kwa nthawi yayitali amayamba kufanana?

Ena amati ndi chifukwa choti amakhala limodzi nthawi zambiri, amaseka limodzi, komanso amayamba kutengera makhalidwe ndi maonekedwe a mnzake.

Koma tikayang'ana Nana ndi Teddy, zikuwoneka ngati akuyamba kufanana kwambiri masiku ano! πŸ˜…β€οΈ

Kodi inu mukuganiza bwanji? Anthu pa chibwenzi amatha kuyamba kufanana, kapena ndi maso athu okha amene amatinyenga? πŸ‘€πŸ˜‚

πŸ“° OpenEye Magazine

🎀✨ KODI MUMAMUDZIWA LV MW? LV MW ndi Afro artist wa ku Malawi yemwe amadziwika ngati wolemba nyimbo komanso woimba. Kupa...
05/06/2026

🎀✨ KODI MUMAMUDZIWA LV MW?

LV MW ndi Afro artist wa ku Malawi yemwe amadziwika ngati wolemba nyimbo komanso woimba. Kupatula luso lake la nyimbo, akupitilizanso maphunziro ake ku Mzuzu University (MZUNI), komwe akuphunzira Bachelor of Science in Value Chain Agriculture.

Kuphatikiza maphunziro ndi nyimbo si ntchito yophweka, koma LV MW akuwonetsa kuti maloto angapo akhoza kutsatidwa nthawi imodzi kudzera mu khama, kudzipereka, ndi masomphenya.

OpenEye Magazine ikupitiriza kuunika luso la achinyamata osiyanasiyana m'dziko la Malawi.

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when OpenEye Magazine posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category