ADMIN WA SANDE

ADMIN WA SANDE WA SANDE YOUR FAVOURITE!!

Mawa pa office 😎
16/05/2026

Mawa pa office 😎

ADMIN WA SANDE Testing TestingπŸ˜‰

Ndinalawilira kuchigayo koma momwe ndawaonera madzi otsukira mphale mmmh bola kumangodya mgaiwa omwewu.Ngati Ukuku ndiku...
22/02/2026

Ndinalawilira kuchigayo koma momwe ndawaonera madzi otsukira mphale mmmh bola kumangodya mgaiwa omwewu.

Ngati Ukuku ndiku area 43, nanga madzi aku area 25 angawoneke bwanji πŸ™ŒπŸ™ŒπŸ€”

16/02/2026

Umatha Daily is trying to hack my page.Kodi munthu samasiya ntchito akatopa?πŸ™„

15/02/2026

Ndizingopita Sunday lokha pa Umatha Daily po munthu ndimakhala ndi zibaba zofuna kukhadzura daily,ndatsekura langa page😌

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ADMIN WA SANDE posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share