Gee Lay Matt

Gee Lay Matt Official Page of Gee Lay Matt
Home of Laughter and Wisdom
0987003381
0896105900

Yatuluka yokha international sound ndiimbireni ngat mukufuna kukhala nawo model my nyimboyi tinvane09870033810896105900N...
23/07/2026

Yatuluka yokha international sound ndiimbireni ngat mukufuna kukhala nawo model my nyimboyi tinvane

0987003381
0896105900

Ntengo ndi 30pin tikufuna akazi awiri

CHIWANDA CHOSOKONEZA OPHUNZIRA WA NZERU.Iyi ndi story yabwino yomwe ikubwera ikamati 7pm madzulo piano.imeneyi itiphunzi...
06/06/2026

CHIWANDA CHOSOKONEZA OPHUNZIRA WA NZERU.

Iyi ndi story yabwino yomwe ikubwera ikamati 7pm madzulo piano.

imeneyi itiphunzitsa mmene tingapewere kusochelesedwa ndi ziwanda

pangani follow Page ino komanso pangani share kuti nkhani zanga zizikupezani mosavuta

Gee Lay Matt

04/06/2026

“KODI MULUNGU AMATIYANKHA MAPEMPHERO ATHU MOTANI NTHAWI ZONSE.”

YOBU 33:14-15.

FOLLOW Gee Lay Matt

14.Pajatu Mulungu amalankhula mnjira zosiyanasiyana,ngakhale munthu sadzindikira dzimenedzi.

15.Mmaloto,mmasomphenya usiku pamene anthu ali mtulo tofa nato pamene akungosinza chabe pa bedi.

Okondedwa mwa Ambuye wathu Yesu Christu,nthawi zambiri okhulupirira amaganiza molakwitsa kuyesa ngati Mulungu amatha kukhala chete.
Izi mochulukira ambiri amaganiza choncho maka pa nthawi yomwe iwowo amapemphera koma sanayankhidwe kapena sanamve kulankhula kwa Mulungu.

Koma dziwani kuti sichoncho komanso sizoona kuti Mulungu amakhala chete.

Mawu amene tawerenga wa kutsimikidzira ndithu kuti nthawi zonse Mulungu amalankhula munjira iyi kapena inayo.

Mutatha kupempherera koma yankho silikubwera,musadere nkhawa nthawi imeneyo Mulungu amakhala akulankhula ndipo akuchita mwa chifuniro chake.

Okondedwa Mulungu sakhala chete ndipo sa zakhala chete pa vuto la munthu amene akhulupirira iyeyo.

Chofunikira mchikhulupiriro basi.Mutatha kupemphera khulupirirani kuti mwayankhidwa kuchokera pamenepo mukhale atcheru ndi omvetsera kwambiri chifukwa:
1.mumayamba kulota maloto
2.kuwona masomphenya
3.kumva liwu la Mulungu
Penanso dzidzindikiro ndi kusautsika kwa mtima ndi maganizo anu pamenepo dziwani kuti Mulungu akalankhula kathu kena.

Ndi munthu amene amakhala chete osati Mulungu.
Ena Mulungu anakuyankhani kudzera munjira zomwe ndafotokodzadzi koma munanyalanyaza.

Mulungu sakhala chete,Mulungu amalankhula nthawi zonse.

Ambuye akudalitseni.

02/06/2026

MARRIAGE IS A COMPETITION

PART 1 ☺️

Maria Anagona yekha mwachifatse pa bed ndipo anaika manja pa chifuwa chake .
apatu Maria anali atayang'ana m'mwamba.
kenako Matt anabwera anamuyang'ana maria ndipo anayamba kumufunsa.

Matt - “Maria kodi chikukuchitikira ndichani?”.

Maria - "Palibe basi kufasa kufuna kuchedza ndi mamuna wanga.

anatero maria uku ataima akumusisita pa chest

Matt -"tasiya zakozi Maria it's not funny tandiyankhe"
anatero Matt uku akuchosa manja a Maria pa chest pake.

Maria - " Eeeh ayi isiyeni imeneyi udakali utsiku kodi tingakambirane kukacha?"

Matt - " Nde wati kukambirana? exactly kukambirana zichani?."

anatero matt akuoneka osakondwa
kenako Maria anamuyang'ana Matt uku akumwetulira"
kenako anayankha.

Maria - " Tikuyembekezera kukhala ndi mwana.

Matt - " Koma tiziti wabalalika eti? kapena waiwala kuti uli ndi mwana wa miyezi 8 basi?"

anatero matt akumuyang'ana Maria mosakhulupilira.
kenako maria anamuyang'ananso Matt modandaula kenako anati.

Maria - " Ndilore ndiyambe kudandaula za zimenezi."

Matt - " OK ndakunva ,kodi tingakambirane mawa zimenezi?

Maria - " Ayi tikambirane lero pompano sindikufuna mawa" ndiponso ndikukufuna utsiku pano."

Anatero Maria uku nkuti akugona mwa tambalale pa bed paja.
"Eish uyu ndi nkazi ochititsa manyazi komanso wamisala" ananong'ona motero Matt kenako anati.

Matt"OK ndiye ufuna ndinene kuti chain?."

Maria - " ungozimangilira Ku denga basi ndizomwe ndusamala"

Matt - "Ndiwe nkazi ochitisa manyazi"

anatero Matt kenaka Maria anaimilira ndipo anati.

To be continued..

please follow my page
Gee Lay Matt

komanso pangani share please

part 2
Loading....

KODI BASI ZINATHA?Nkazi wanga anapeza ntchito .ndipo bwana wake anali waku China koma mamuna (Chinese man 💼🇨🇳  )Koma osa...
01/06/2026

KODI BASI ZINATHA?

Nkazi wanga anapeza ntchito .
ndipo bwana wake anali waku China koma mamuna (Chinese man 💼🇨🇳 )

Koma osanama nkazi wanga atangoyamba kugwira ntchito kwa nkuluyu zinthu zambiri zinasintha ndipo zinkatiyendera kwambiri .
osanama bwanayu ankatithandiza pachilichonse .
Kenako nkazi wanga anatenga mimba ,ndipo patadutsa nthawi anakhala ndi mwana👶

Kenako bwana wa nkazi wanga anabwera kuzamuona mwana wathu komatu anali atatigulira mphatso zambiri za mwana......

kodi mwanayu bambo wake anali ndani?
pangani follow Page yanthu Gee Lay Matt kuti munve mmene zinathera.

moti basi zinatha?

To be continued..

01/06/2026

Tchulani mistake imodzi yomwe munapangapo mmoyo mwanu kuti wina wake asazapangenso idzamubweretsera mavuto✅
follow Gee Lay Matt

Address

Khwethemule
Makwasa

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Gee Lay Matt posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share