BRUNO

BRUNO Kuphunzisa + kudziwisa + kucheza = hophop blog

Mmmh iwe mkumati ka bele loyima koma atachita kuvala
11/03/2025

Mmmh iwe mkumati ka bele loyima koma atachita kuvala

10/03/2025

Mumakhala mwadya nokha Ku mbanda kucha,ife tikamadya inu muli pompo,zimakunyasani why?ngati zanuzo mammawawo munatiwelengela

Apa nde talandilidwa mukuona bwanji mikozi?
09/03/2025

Apa nde talandilidwa mukuona bwanji mikozi?

Akamati mutu wa nkhani,amanena umenewu.
09/03/2025

Akamati mutu wa nkhani,amanena umenewu.

Mbewu imeneyi itamukwatila mlongo wanu,inuyo mungamve bwanji?
08/03/2025

Mbewu imeneyi itamukwatila mlongo wanu,inuyo mungamve bwanji?

07/03/2025

Mukadikila ukwati oyela muchedwa,tangololani ukuda omweu uzikayelela mutalowa kale banja.

05/03/2025

Enanu mukusala kudya koma mukumadya mobisa cholinga anzanu asakuoneni,kaya ndiye mukuzivutisilanji?

Ineyo ndi iweyo tili Ku nyanja thawi Imeneyo
05/03/2025

Ineyo ndi iweyo tili Ku nyanja thawi Imeneyo

Chitetezo kuposa Ku bank
05/03/2025

Chitetezo kuposa Ku bank

05/03/2025

Pa katoni ya Colgate kujambulapo mano koma pa katoni ya ma pad osajambulapo kanthu,ai zikomo

Address

Mangochi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when BRUNO posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share