
24/09/2025
ππ₯ *MWAMBO WOTSEKULIRA MZIKITI*π₯π«
***A MOGWIRIZANA NDI KOMITI YA *SAITI M'GAWE MASJID* AKUDZIWITSA ANTHU ONSE ZA MWAMBO OTSEKULIRA MZIKITI OMWE UCHITIKE MOTERE:
: LOWERUKA PA 27 SEPTEMBER 2025π
π² π²:*SAITI M'GAWE MASJID T/A MAPIRA KU NASENGA M'BOMA LA MANGOCHI*
β² : KUYAMBIRA *10 KOLOKO KUMMAWA MPAKA NTHAWI YA ASR*
π»π€OLALIKIRA π π₯ *SHEIKH *ππ₯π₯ *SHEIKH *π₯
KOMANSO AKATSWIRI PANKHANI YOLAKATULA MA VERSE π₯ *MINIKAA π₯* NDI π₯ *π₯
KUMENEKU TIKAKHALANSO NDI π₯ *π₯
πͺπͺ *MULENDO OLEMEKEZEKA*πͺπͺ
π₯ *ACHAIRMAN AMUSLIM ASSOCIATION OF MALAWI HIS EMINENCE SHEIKH *π₯
*OSANGALATSA ANTHU PATSIKUNDI *π₯ KOMANSO π₯ *
MUKAFUNA KUMVA ZAMBIRI IMBANI FONI PA MANAMBALA AWA:
*0887753896* (SH ADAM M***A ) KAPENA 0897262998 (Brother Yusuf)
*TIYENI TIKAKUMANE KUMENEKU INSHAALLAH*
Program yonse izakhala live pa *π«1islamTv page*