06/09/2024
Convention ya chipani cha PP chili ndi mipando yokwana 16 yomwe akuti alowa ndi Mutu popanda opikisana naye Monga president wachipani ndi DR Joyce Banda Komaso ma Vice President amzigao zonse ndi omwe akalewo