PaMudzi

PaMudzi Home of ntertainment and news

27/09/2025

Zoopsya ku Mulanje.

27/09/2025

Kodi guys, zibwezi zomajambulitsa nazo ma video limodzi mukumazitenga kuti?

Anthu awiri omwe sakudziwika maina apezeka atafa pafupi ndi pokwerera Galimoto za limbe. Anthuwa akuganiziridwa kuti aph...
27/09/2025

Anthu awiri omwe sakudziwika maina apezeka atafa pafupi ndi pokwerera Galimoto za limbe.

Anthuwa akuganiziridwa kuti aphedwa nthawi yomwe amaba ma cable a phone pafupi ndi malowa

27/09/2025

Happy Sabbath
πŸ™πŸΏ

26/09/2025

Uyu wabwera ndi molalo uyu πŸ˜‚πŸ™ŒπŸΏ

26/09/2025

Nurse kukhosomola kuposa patient
πŸ˜‚

24/09/2025

Mchinji kwachema

24/09/2025

Current situation ku Mchinji Boma, anthu Boma alilandira ili ee.
Simmene kuliri. Wadya ntoliro.

Congratulations Biggy, Titumikiren
24/09/2025

Congratulations Biggy, Titumikiren

24/09/2025

Sibasi tichezereno apa
πŸ•ΊπŸΏπŸ’ƒπŸΏ

24/09/2025

Ma poster otamanda mtsogoleri wakale wa dziko lino a lazalasi chakwera ayamba kuchotsedwa mu Lilongwe

Address

McHinji District

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00

Telephone

+265886901904

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when PaMudzi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share