27/10/2025
NCHE updates
Question;1. what's the difference between ODeL and generic
โma students omwe amasikhiridwa ku university by NCHE koma generic. Ma students amenewa amakhara manja mwaboma( support comes from the government) fees IMAKHARA yochepa komaso OPHUZIRA amenewa amapatsidwa loan ndi a loans board Malawi plus upkeep ya semester yonse which is 580,000 komaso uphuzira omwe asakhiridwa generic amaphuzilira pa campus pa university pomwepo plus kugona pompo ndi kugwiritsa ntchito Library mosavuta
โ Pamene OPHUZIRA yemwe wasakhiridwa ku ODel sakhara manja mwaboma , salandila nawo loan from loans board, salandila nawo upkeep, saphuzirira pa campus thawi zambiri amaphuzira through online, fees amapereka modura kusiyana ndi wa generic, komaso most times sakharila pa campus ya university this is 99%
โfollow up this page kuti next update ya NCHE tingapange post isakuphonyeni soon ndikamba zokhudzana ndi a loans board malawi maconditions awo
stay tuned